Listen to Shame on You (feat. Blacka Fella) by MartseMw

Shame on You (feat. Blacka Fella)

MartseMw

Hip-Hop/Rap

716 Shazams

Lyrics

Hater a who da dem hater can hate Martse Nah, made da dem from elderly to pikini Can you know nonse that Martse imani hip-hop don dada Wah dat taona, choka sowa Nanga ndichani m'mafuna Amalawi Adani anga amakondwa mkamapempha Samasangalala za ine zikamayenda Amabweletsa ice mkayamba kutentha Kundipanga blindfold ndikamapenya Makape ena amazitcha anzanga Pansi pa mphasa akusunga lupanga Alipo iye wosunga moyo wanga Mafana mwachepa mukavale ma pamper Ati ti-mamwa zotchipa, imwa zodulazo Ati sitimatha kuyimba, imba yotchukayo Osama hater ghetto ikatifila I'm only 24 koma ndikuyimilira Ndachokera kutali kuti ndipeze zonsezi Nde poti ndangoyamba mukukwiya ndi zomwezi Team yaine siyimasewela ndi ana First prince on this structure kuzijaja Zopemphelera adani anga sindupanga nawo, no-no-no Ndukuwuzani sindupanga nawo, nah Zopemphelera adani anga sindupanga nawo, no-no-no Ndukuwuzani sindupanga nawo, nah So if you hatin' on me mfana, shame on you Ukufuna tisabole mfana, shame on you Ukufuna tisawuke mfana, shame on you Shii, back to sender, shame on you Tichepetse zomayesana Zomandiyankhula kuti munditole mkamwa Osamakwiya ndi ngini yoti ndi yanga Nanu wekani harder Jah Jah amayankha Fresh man, ndaona zikhomo nde ndafila pain yeniyeni Quarter yama loss kupanga ma gain eni-eni Mafana mwamasuka mufunika chain Kuyipitsa mbiri ya ine ndi yanu ganyu Amazifila ndi wamatama sanandionepo N'namuyankhula sanandiyankhe, nan'nathokepo Amamufuna girlfriend wanga Asa choka ndilinaye wanga wamva No long talk ndakuyika pa pause Ndisanakudye makofi photo tenga chimodzi Kusaka ma move aine from day by day Akamableya amandilota mafanawa m'ma gay Zopemphelera adani anga sindupanga nawo, no-no-no Ndukuwuzani sindupanga nawo, nah Zopemphelera adani anga sindupanga nawo, no-no-no Ndukuwuzani sindupanga nawo, nah So if you hatin' on me mfana, shame on you Ukufuna tisabole mfana, shame on you Ukufuna tisawuke mfana, shame on you Shii, back to sender, shame on you Olo nonse mutabwela gulu lonse Martse complex, we run this office Mu ghetto kuwawa ase, fotseki (ha-ha-ha-ha) One time Kabu, Gaza Ben Raz Sir Jevo trip on me
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out