Lyrics

Sembe umoyo ogula Sembe kuliye kuti tinalinawo Eti siya Mwana wanga Ziko la vuta Antu nawo alimba mutima Matenda nayo Siyo sila Mwana wanga Ziko la vuta Antu nawo alimba mutima Matenda nayo Siyo sila Nizaku wuza bwanji Kuti umve Kuti umvele Mwana Nizakuwuza bwanji Kuti umve Kuti umvele Mwana Mwanaaa Mvela mvela mvela mwana Mawe mwana Mvela mvela mvela mwana Mawe Uzi sungile weka umoyo wako Uyu moyo sugula Uka tayika sungautole Uzi sungile weka umoyo wako Uyu moyo sugula Uka tayika sungautole Mvela mvela mvela mwana Mawe mwana Mvela mvela mvela mwana Mawe Uzi sungile weka umoyo wako Uyu moyo sugula Uka tayika sungautole Uzi sungile weka umoyo wako Uyu moyo sugula Uka tayika sungautole Uyu umoyo sogula Ukawu taya kuliye kuti Ni wutole soti Mwana wanga Uzini mvelela Ni chifukwa chabe niku konda Kulibe wina anso Azaku wuza mwana wanga Uzini mvelela Ni chifukwa chabe niku konda Kulibe wina anso Azaku wuza Niza chita bwanji Kuti umve Kuti umvele Mwana Niza chita bwanji Kuti umve Kuti umvele Mwana Yeah ehhh Mvela mvela mvela mwana Mawe mwana Mvela mvela mvela mwana Mawe Uzi sungile weka umoyo wako Uyu moyo sugula Uka tayika sungautole Uzi sungile weka umoyo wako Uyu moyo sugula Uka tayika sungautole Mvela mvela mvela mwana Mawe mwana Mvela mvela mvela mwana Mawe Uzi sungile weka umoyo wako Uyu moyo sugula Uka tayika sungautole Uzi sungile weka umoyo wako Uyu moyo sugula Uka tayika sungautole Sembe umoyo ogula Sembe kuliye kuti tinalinawo Eti siya Mwana wanga Ziko la vuta Antu nawo alimba mutima Matenda nayo Siyo sila Mwana wanga Ziko la vuta Antu nawo alimba mutima Matenda nayo Siyo sila Nizaku wuza bwanji Kuti umve Kuti umvele Mwana Nizakuwuza bwanji Kuti umve Kuti umvele Mwana Mwanaaa Mvela mvela mvela mwana Mawe mwana Mvela mvela mvela mwana Mawe Uzi sungile weka moyo wako Uyu moyo sugula Uka tayika sungautole Uzi sungile weka moyo wako Uyu moyo sugula Uka tayika sungautole
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out