Featured In

Credits

COMPOSITION & LYRICS
lovemore majuta
lovemore majuta
Songwriter
Lonjezo Banda
Lonjezo Banda
Songwriter
Hopeson Mzembe
Hopeson Mzembe
Songwriter

Lyrics

Yah, palowa njoka pano ndiye mkundifunano Palowa njoka pano ndiye mkundifunano Dzuloli mwandithila thope pakanjinga kanu Dzana dzanali munangondidutsa pakanjale kanu (palowa njoka) Palowa njoka (palowa njoka) Palowa njoka (palowa njoka) Palowa njoka (palowa njoka) Palowa njoka (palowa njoka) Palowa njoka (palowa njoka) Palowa njoka (palowa njoka) Palowa njoka (palowa njoka) Palowa njoka Amakufuna zikakhalatu zawavuta (yah, yah, yah, yah) Yah, amakufuna zikakhalatu zawathina (yah) Yah, koma ku party umva asabwere amene aja ndachamba (yah) Koma ku ukwati umva asabwere amene aja ndamowa (Oh, my God) Yah, palowa njoka pano ndiye mkundifunano Palowa njoka pano ndiye mkundifunano Dzuloli mwandithila thope pakanjinga kanu Dzana dzanali munangondidutsa pakanjale kanu (palowa njoka) Palowa njoka (palowa njoka) Palowa njoka (palowa njoka) Palowa njoka (palowa njoka) Palowa njoka (palowa njoka) Palowa njoka (palowa njoka) Palowa njoka (palowa njoka) Palowa njoka (palowa njoka) Palowa njoka Yah, amafuna uzivutika Amafuna uzingopempha Amafuna uzisawuka Inenso ndekha ndisamapushe, yah, yah Pano panalowa njoka Ka banja kajaso kanatha, panalowa njoka (palowa njoka) Palowa njoka (palowa njoka) Palowa njoka (palowa njoka) Palowa njoka (palowa njoka) Palowa njoka (palowa njoka) Palowa njoka (palowa njoka) Palowa njoka (palowa njoka) Palowa njoka (palowa njoka) Palowa njoka Yah, yah, yah, yah, yah Yah, yah, yah, yah, yah Panopa panalowa njoka (panalowa njoka) Panalowa njoka (panalowa njoka) Panalowa njoka (panalowa njoka) Panalowa njoka (panalowa njoka) Panopa panalowa njoka (panalowa njoka) Panalowa njoka (panalowa njoka) Panalowa njoka (panalowa njoka) Panalowa njoka (panalowa njoka) Panopa panalowa njoka, rr Yah, yachina Seven adah
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out