Lyrics

Talikila, talikila Talikila, talikila Ndati talikila, talikila Talikila, talikila Samakondwa zikamayenda, zikavuta kusekelela Chilichonse ungapange basi busy kukhomelela From Monday to Sunday, busy kusatila Amakhala kuti, ndindani, amapanga chani eish Samakondwa zikamayenda, zikavuta kusekelela Chilichonse ungapange basi busy kukhomelela From Monday to Sunday, busy kusatila Amakhala kuti, ndindani, amapanga chani Eish Munthu ndi njoka njoka Osakomedwa naye, sekelela ndikudyele osakomedwa naye Munthu ndi njoka njoka Osakomedwa naye, tembenuka ndikulume osakomedwa naye Munthu ndi njoka njoka Osakomedwa naye, sekelela ndikudyele osakomedwa naye Munthu ndi njoka njoka Osakomedwa naye, tembenuka ndikulume osakomedwa naye Munthu ndi njoka njoka Munthu ndi njoka njoka Munthu ndi, munthu ndi njoka Munthu ndi, njoka!
Writer(s): Robert Ching'amba Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out