Lyrics

Cheo Meek (Kukonda ma bodza) (Umakonda ma bodza)(iwe) (Kukonda ma bodza) (Umakonda ma bodza)(ine) (Kukonda ma bodza) (Umakonda ma bodza)(ife) Numbers don't lie koma (bodza ndi labho) Sindikunamizani guys koma (bodza ndi labho) Wapulumuka kangati ase? (ndibodza lakolo) Kusekelela za bodza koma kukwiya ndi chilungamo (ndi chilungamo) Iwe Numbers don't lie koma (bodza ndi labho) Sindikunamizani guys koma (bodza ndi labho) Wapulumuka kangati iweyo? Kusekelela za bodza kukwiya ndi chilungamo (ndi chilungamo) I wish you more life ndi zi good health Bodza ndi la bho koma don't lie to yourself Titalke ma facts bwanji apa uwone ulire Practice makes perfect sunganame usana chalire Wamenya call Ku vephi kuti sukufika bho Ukunama Mesa umangofuna Ku chilla ndi boys Out here asking for the truth Koma you already know Kuti bodza laku saver wa dodger chilungamo Pa CV pa dzadza ma bodza (bodza) Ma dolo kunamiza ma zoba (Zoba) Akunama kuti Aku baller (baller) Koma Ali paden kungopola (bodza) Koma akuzinamiza okha (okha) Ife trap ili makola (Ife you love me) Babe chilungamo pena chimazakola Pena ndimazanama kuti ulipo wekha (Bodza ndi labho) Sindikunamizani guys koma (bodza ndi labho) Wapulumuka kangati ase? (ndibodza lakolo) Kusekelela za bodza koma kukwiya ndi chilungamo(ndi chilungamo) Iwe Numbers don't lie koma (bodza ndi labho) Sindikunamizani guys koma (bodza ndi labho) Wapulumuka kangati iweyo? Kusekelela za bodza kukwiya ndi chilungamo (ndi chilungamo) (Infectious) Ati I love you Ndili ndi cash a ma bodza a bho Akazi onsewa nda bonzapo Afana ofewa cap ngati wavala chipewa Koma boys ati ndaba disposable Ndikuchita kusowa response ya bho Olo jokes pa mikozi po Ati dende the boys get toasted Roasting beats and beef Of course and some shots been dropping See the way we run the streets They dropping off like leaf we smoke them Got me coughing Some go deep like the ocean we floating You know what it is the clan is chosen bro Don't lie koma (let's go) Sindikunamizani guys koma (let's go) Wapulumuka kangati ase? (ndi bodza lako) Kusekelela za bodza (ndi chilungamo) Iwe Numbers don't lie koma Sindikunamizani guys koma Wapulumuka kangati iweyo? (ndi bodza lako) Kusekelela za bodza kukwiya ndi chilungamo (ndi chilungamo)
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out