Lyrics

Ayo- Mtima Ukungogunda Mtima Ukungogunda Mtima Ukungogunda Ayo Landie (Ungogunda) Yah The way she love me zachilendo Kavala bandana kandipeza pa bando (Yeah) Kali cool ndima Frenzo Kamatha Ku mixer ndi kupota mtondo Mkazi wa trapper Iwe ndi mkazi wa trapper Mkazi wa trapper (Kas) Mkazi wa trapper wangoposter lero (Uh Huh) She was holding a blunt zinamubanda yeyo (Huh) (Woah) Mkazi wa trapper ndi Ka gangster girl (Uh Huh) Ndika snake ndika slime (Uh Huh), Kangovalaso belo (Huh) (Oh Ho) Mkazi wa trapper ndi trapper Mkazi wa trapper ndi slime (Slatt) Akati abwera m'mawa kadya ma blunt nine (Nine) Kafuna kuvaya mawa ati sinkhala online (Nah) Mkazi wa trapper amachena amakonda Nike (Yea) Yeah The way she love me zachilendo Kavala bandana kandipeza pa bando (Yeah) Kali cool ndima Frenzo Kamatha Ku mixer ndi kupota mtondo Mkazi wa trapper Iwe ndi mkazi wa trapper Mkazi wa trapper Mkazi wa trapper ndi wo trapper mtima (mmh hm) Hotel standard wefu wefu, Siza m'chimanga (M'chimanga) Sizongochoka kwanu mkumati ndimaka (No) Sungandibele olo utakhala ndi mkaka (Bwoo) Kakufuna ma kiss, Netflix and chills Tikusuta ma cheese, kakamayenda sungakayimitse Makape akati aka disse, ndichi Mponela ngati Madise Kama sipaso zima baby Gin (Gin, Gin, Gin) Kali ndi Kas koma Ndine amene ndiku kapanga Du-du-du-du-du Du-du-du-du-du Zachilendo Ndikupota Mtondo Mkazi wa trapper Iwe ndi mkazi wa trapper Mkazi wa trapper Iwe ndi mkazi wa trapper Mkazi wa trapper Mtima Ukungogunda Mtima Ukungogunda
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out