Lyrics

Ndikavunga Text Umachedwa kuyankha Ukavunga Message Pompo Ndimayankha Ndikaimba Phone Ngati Sukufuna Kuyankha Ngati Sukufila Unaka Talka Ndizingoyaka Gangster ali Single! Bola Ndingokhala Single Ndizingoimba Nyimbo Ya Gangster ali single Umangot Vepi Bwanji Sungatenge Tchuthi Ndagwila phone Yako wazizidwa ulibe Juzi? Zosathoka Zomwe ndalakwisazo Ndizachimidzi Ndili Serious siza Lucious koma play me si Jacuzzi Unena Bwanji kuti You With me,when u Texting other Niggas Naneso Sindingasibise Ndatopa with your Shenanigans Kumandiika Ntika Koma Uli Pa Nsika Ine ndi Business Man Zokwera ndimazitsika Mwina ukufuna G wabanja Or ungofuna mwana Koma Mnakuuza kale kuti udekhe ndingo Hasa Ndiwe Mkazi wa Trappa Ndizakupasa Ma Pasa Ndikupasa Mapasa Ndizakuoasa Mapasa Ndizakupasa mapasa Ukakwiya simandimafila bho ndipange admit I like it when we cool ngati Salifornia Breeze Ma babe ena onse basi Ndawapanga Delete Pachi G i'm just Trynna Show u kuti you tha one for me Koma Ndikavunga Text Umachedwa kuyankha Ukavunga Message Pompo Ndimayankha Ndikaimba Phone Ngati Sukufuna Kuyankha Ngati Sukufila Unaka Talka Ndizingoyaka Gangster ali Single! Bola Ndingokhala Single Ndizingoimba Nyimbo Ya Gangster ali single
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out