Listen to Koma Boys (feat. Ace Dirty & Krazie G) by Crispy Malawi

Koma Boys (feat. Ace Dirty & Krazie G)

Crispy Malawi

Hip-Hop/Rap

53 Shazams

Lyrics

Koma boys Ayo Nihilo bring the beat son haha Zomwe imapanga boys ina Isakuone ukuvina Koma ukulira (Hihihhihi) Kundibela lighter ntakubanditsa(aah) (koma boys) Kundibela phone ntakuyakitsa(aah) (koma boys) Pamaso kuchiller kumbali Ku disser(aah) (koma boys) Kubwera pa den kundikalipitsa(aah) (koma boys) Tisamavetsana kuwawa Tizimvetsana kukoma boys Kuyikana mkati Osakankhirana mpaka Ku khoma boys Kumagawanako wezi wezi Osamaphangira boys Slow paced kuvaya Ku front (Tsitsa Pang'ono) Osathamangira boys Kundikweza kuzanditsitsa Mbiri yanga mumayipitsa Mumafuna zabwino zonse zikhale zanu Mukuwona moyo Kumandiyenda mbali ngati nkhanu Kumbali muku hater pamaso kuonesa mano Kufuna kulanda mkazi wanga (koma boys) Kundiponda Ka dollar kanga (koma boys) Osakapeza kamtima mumafuna zoyambana Pano ndikuoanga zanga Pano tinadana Krazie tsitsi lako walitani? Ukubanda grade yanji? Ma trainer ngati njanji Ungobanda Zi mbanji (Zi m'banji) Kwa chigulu changa ine ndina lonjeza Tizizangoyaka Ku chaser ndi kombeza Kona drip yanga ilitu thelele ikuteletele Tele tele Tele tele yeahhh (Koma boys) Kundibela lighter ntakubanditsa (aah) (koma boys) Kundibela phone ntakuyakitsa (aah) (koma boys) Pamaso kuchiller kumbali Ku disser (koma boys) Kubwera pa den kundikalipitsa (aah) (koma boys) Tisamavetsana kuwawa Tizimvetsana kukoma boys Kuyikana mkati Osakankhirana mpaka Ku khoma boys Kumagawanako wezi wezi Osamaphangira boys Slow paced kuvaya Ku front Osathamangira boys Zomwe umaithokz boys Anyway osamafooka boys Tixakukoka ma Balls Kukakuponya Ku falls (Zomwe imapanga boys ina) (Isakuone ukuvina) (Koma ukulira) (Koma boysss) (Koma boysss)
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out