Lyrics

(Timothy Got the Fire beats no matter what it is) (Ayo Landie) Ukamva Gu! gu! Gu! Gu speaker yakwa neighbour Gu! Gu! Gu! speaker yakwa neighbour Gu Gu! Gu! speaker yakwa neighbour Ukamva! Slatt Kwabwera smokey Ndi Themba Samaona kuti lero ndi lolemba Kungodya ma Zaza ntibu tangokweza Playlist ya DJ neighbor suzayiloweza Chotsa ti nyimbo tako faka Crispy ndi Krazy Za alamu anu ukamufunse Celba ndi Zeze Brainlock in the mix itsitse ikweze Ndili ndi chi keys chi Jeff isokoneze Kwathu kumveka Nyimbo Kwa neighbour kumveka nyama Chispeaker kukopa fanz amayesa ngati ma scammer The way I do my dance ngati MC Hammer Speaker tangokweza nde today mu runner Ndikudya Ka loud sound ili low Ayy Tandipatse cow kuti ndivine ngati nyau She send me little letter She says she's getting better I'm never under pressure Chi speaker ndangokweza Ukamva Gu! gu! Gu! Gu speaker yakwa neighbour Gu! Gu! Gu! speaker yakwa neighbour Gu Gu! Gu! speaker yakwa neighbour Ukamva! Speaker yakwa neighbour indiboola makutu Kungochoka vep akut speaker ituluke Ungodina next uwone akutulutse Kuti Gu!Gu!Gu!Gu! Mpakana Kuche Kukanika kubleya man Ma window kutseka blaz Azimayi kuchola dance,ma babe Ku twerka man Muno ndimu hood mwanga wina andinyumwitse Yesa zida phwanga uwone fanz ikuwukire Neighbour ziphokoso Ndi Yambisa nkhondo Ndivaya Ku popo Ndivaya konko Neighbour ziphokoso Yambisa nkhondo Vaya Ku popo Vaya konko Ah speaker yakwa ikati isokosere Imakhala full blast basi asokoneze Ndichi ntibu makina chimphaso makoswe Koma De-Fra basi ndiyi bongose Daily kwa neighbour ngati kuli ma demo Iwe kufa makutu ngati wasonkha ya memo Neighbour samamva za munthu Iyeyo ndi wa ghettoSpeaker yake inathawa nawo mazeno Neighbour Neighbour umatiwonjeza Neighbour Neighbour pajatu ndinalonjeza Koma tangowona sound yako wayikweza Neighbour Neighbour Neighbour Neighbour suzatheka Ndazuka chifukwa cha noise Speaker yakwa neighbour imeneyo Ingolongola wangokweza Zima 808 Wayamba chama quarter to Pano ili past two Ndikungomva gugugu wandisokoneza Mutu Iwe Neighbour bwanji ukukweza sound Ngati ndi December Wayamba kale kale kuthoka sukuleka Sound ili loud ngati Zaza ndi kukhwemba Umandijayila tsiku lina ndizakukwenya Uzandimva ndikanena Pano sumakhala wekha Makufila ndiwe neighbour Koma nzakutopela Ndikabwera kupeza sound wakweza Kuli ana akufuna kubleya Speaker yakwa neighbour imandisokoneza peace Zoti ndimableya ndangodzuka Ku roller spliff Ti ana tingodabwa kodi Ali kut Sticx Moto sungayake opanda iyeyo call him please Ndinali Ku pharmacy kugula Kaye mazza Themba Ali ndi sprite Crispy Ali ndi Zaza Magetsi akathima neighbour Ali ndi generator Zoma flexer ka Mwana kake amandiletsa Koma boys sizamva ndili naye Ku corner Eko Ka gram Kalitchetche ta roller Kukonda Zima speaker ngati ma sister Ku culture Nditha kukagona konko mpaka kukacha
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out