Listen to Tuno (feat. Crispy Malawi) by King Tuzi

Tuno (feat. Crispy Malawi)

King Tuzi

Hip-Hop/Rap

653 Shazams

Lyrics

"Amwene" "Amwene ineyo ndikangomulingalira Tuno amwene" "Ehe ukamulingalira Tuno chimachitika ndi chani (AB-Dul with the Sauce) "Ndikangoti ndimuganizire Tuno amwene" "Ukangoti umuganizire Tuno chimachitika chani?" "Iwe tayankha eh" "Tasiya kubanda Tayankha" "Amwene golide amwene golide eh Tuno amwene" "Golide wotani?" "Ndikangoti ndimulingalire Tuno amwene" (Ayy) "Ndikati golide yokhayo" (Ayy) (Ayy) Ndapota Ka spliff kukayatsa (eish) Kundilowa mphuno (utsi) (amwene) Ndaona chimkazi (mmh hm) ali welo (mmh hm) Ndikufunika chi cross ngati Bruno (ndipatsile chi cross) (Ayy ay) Ndilipa magobo daily Osamabwelela mbuyo (Osamabwelela mbuyo) They were sleeping on me now a mwayi adzuka Koma ena akadali mtulo I got a confession I'm crushing on Tuno (eish) (Eh) (Eh) Tuno!(eh) Tuno! (koma Tuno Ase) (amwene) (mmh) Tuno! (Koma Tuno Ase) Ndati Ndaona chi mkazi ali welo Kufunika chi cross ngati Bruno (eh amwene) Chi chick cha bho ngati afuna banja (eish) (eish) Muwuze Andipeze Kuno (tiye nazo) (Ayy) (Ayy) Tuno Amwene (amwene) ntagwira uyuyu ndingapenge (ndingapenge) (eish) Ma member ati ndumayabwa Akangomva da king ngati aponda chitedze (ngati ndaponda chi cha?) Tuzi Ku flopper man sizingatheke Ndayenda ndi Ganja ndukakwera ndege Zosatheka Ndimapusha zitheke She[?] didn't want to feature these rappers keep begging (Let's go) Ndine mfana wofewa (ofewa) Nsima ndimamwera Fanta (Fanta) Koma sumandisala spaghetti (sumandisala) Ndine mfana wozungiza bongo Rasta Sindiwopa kuvaya ku ndende (sindiwopa kuvaya) Koma ndendende Sakumvetsetsa I'm stoned Ati ah ukufuna umgende? (Ah) Zandi Wenger ngati coach wa Arsenal Muyimbire Spe afika anditenge (muyimbire Spe) Ndati Tuno alikuti? (Alikuti) In the trap see the way I be rapping They say I'm the goat ati Tuzi ndi mbuzi (sikunyoza ayi) Lil shorty bad and she boujee Let her meet the fam Kudzamutenga kumudzi And I just hit another but no dey ain't no strings attached Palibepo ulusi (palibepo Ka cha?) Ndili pa TV pa news (uti bwa?) I'm the goat when it comes to the music Ndapota Ka spliff kukayatsa (eish) Kundilowa mphuno (utsi) (amwene) Ndaona chimkazi (mmh hm) ali welo (mmh hm) Ndikufunika chi cross ngati Bruno (ndipatsile chi cross) (Ayy ay) Ndilipa magobo daily Osamabwelela mbuyo (Osamabwelela mbuyo) They were sleeping on me now a mwayi adzuka Koma ena akadali mtulo I got a confession I'm crushing on Tuno (eish) (Eh) (Eh) Tuno!(eh) Tuno! (koma Tuno Ase) (amwene) (mmh) Tuno! (Koma Tuno Ase) Ndati Ndaona chi mkazi ali welo Kufunika chi cross ngati Bruno (eh amwene) Chi chick cha bho ngati afuna banja (eish) Muwuze Andipeze Kuno (eish) (Ayy) (Ayy) (Malawian) Uli ndi Thako kapena umangotha kugwedeza chiuno(hmm?) Kuyika dollar pa table kuti ndikutengere Ku bedi ngati tulo Koma sindikuthoka iweyo Tuno Ndikufuna nzako wachi mbuyo (wachi mbuyo) Ati Spe ma babe umangosintha ngati kicks Kodi umamenya Judo? Hmm Keep it going keep it moving (vroom vroom) Ngati sizikuyenda yatsa ma hazard Zathu zikuyenda tika dropper anthu amangoti ah za Hard (waona) Zili fly ngati nthakati Ku north,kumwera ndi pakati (yeah) Been a player kwa zaka zaka Pano level yangayi ndi ya Lampard Ma drinks titha Ku shoppa Ma Mogo amandipweteka mphuno (mmh) (Tuno) Utha kushala panja Ukapota spliff ndi kuzayatsila muno (Tuno) Koma Na lero olo Nepman sanakambaso za Dzulo?(No Way) Ife nde tili mkati Uli panja udya bench ngati ukunyamula zitsulo (Yeah) Ndapota Ka spliff kukayatsa (eish) Kundilowa mphuno (utsi) (amwene) Ndaona chimkazi (mmh hm) ali welo (mmh hm) Ndikufunika chi cross ngati Bruno (ndipatsile chi cross) (Ayy ay) Ndilipa magobo daily Osamabwelela mbuyo (Osamabwelela mbuyo) They were sleeping on me now a mwayi adzuka Koma ena akadali mtulo I got a confession I'm crushing on Tuno (eish) (Eh) (Eh) Tuno!(eh) Tuno! (koma Tuno Ase) (amwene) (mmh) Tuno! (Koma Tuno Ase) Ndati Ndaona chi mkazi ali welo Kufunika chi cross ngati Bruno (eh amwene) Chi chick cha bho ngati afuna banja (eish) Muwuze Andipeze Kuno (eish) (Ayy) (Ayy)
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out