Lyrics

Tayima Kaye tayima kaye tayima kaye tayima kaye tayima kaye Ndinabettera success ndiku winner Ndiku winner ndikupanga Rebet Ndilibe Ex Koma ngati Alipo mwina (Umfila ndani?) amapanga regret Umafila ndani? Hahaha Ati amafila Spe Atha kuyimba nyimbo zonse analoweza Tape Ndangokhala Phee! Ndikufuna ndimumvere Fanbase yangodzadza ndi ma babe Boys singasiye kufila Spe Simangomvera nyimbo imapanga relate It's all love apapa palibepo hate Nde aliyese pamalo pake (Pake pake pake pake pake) Aliyese pamalo pake (Pake pake pake pake pake) Aliyese pamalo pake (Pake pake pake pake pake) Aliyese pamalo pake (Pake pake pake pake pake) Aliyese pamalo pake (Pake pake pake pake pake) Pake Pake Game ili pachi make, chilichonse chili Malo mwake Homie Sali stuck koma akufuna ndimukankhe That's my dawg sangandilume nde sindingamuthawe Olo ntakhala pa zero iwe dollar sindingakukawe Bola when I make it double zisazakuwawe We're on the road tikupanga money ngati katangale Sizambiri koma zokwana ine ndi A'bale I don't wanna die before I live my dreams Lord knows how bad I wanna make these M's Ku runner game with a milli on my name Siza Drake koma life was never the same Pano Ha! Ati amafila Spe (Spe!) (Spe!) Atha kuyimba nyimbo zonse analoweza Tape Ndangokhala Phee! (Phee!), Ndikufuna ndimumvere (Mvere) Fanbase yangodzadza ndi ma babe Boys singasiye kufila Spe Simangomvera nyimbo imapanga relate It's all love apa Palibepo hate Nde aliyese pamalo pake (Pake pake) Pake pake pake pake (aliyese pamalo pake) pake pake pake Pake pake pake pake pake pake pake Pake Pa Pake pake pake pake pake pake pake Pake pa Pake pake pake pake pake pake pake Aah! Ndinabettera success ndiku winner Ndiku winner ndikupanga Rebet (je map'elle Spe) (International Spe)Yeah Ndilibe Ex koma ngati Alipo Mwina amapanga regret Yeah Brrr! Brrr! Brrr! Gang! Brrr! Brrr! Brrr! Gang! gang! gang! Hahaha Ndilibe Ex koma ngati Alipo (Malawian) Mwina amapanga regret Yeah chilichonse Malo mwake? Hahaha wakafila bwa? Ukudziwa kale Aliyese pamalo pake Aliyese pamalo pake Aliyese pamalo pake Aliyese pa- Pako Krazie G
Writer(s): Chifundo Chingaipe Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out