Music Video

Zibwente (feat. Dette Flow, Crispy Mw, Nitrix)
Watch Zibwente (feat. Dette Flow, Crispy Mw, Nitrix) on YouTube

Featured In

Credits

PERFORMING ARTISTS
Phyzix
Phyzix
Performer
COMPOSITION & LYRICS
Phyzix
Phyzix
Songwriter
Asodzi
Asodzi
Composer
BFB
BFB
Composer

Lyrics

captain bae Kwa ma hope anga amagulisa zibwente Broz yake imakonda ma cartoon a ben 10 Ndikafuna ku chiller Ndimatenga dollar ya zibwente Ndi chilichonxe cha Ben 10 Ndikatelo am in skueeww Kudya kudya kudya kundya kudya Zibwente(Turn up)×4 Yoooh Amaoneka sizimamukhuza Zoti ndine mfana otchuka Amaoneka sizimamisutha Olo number yake amakaniza ... Koma zibwente zokhazo nde ndimagula Kuti mwina nthawi yochiller naye izichuluka Ndine captain bae Bae wako ndi bae chabe Ndine captain bae Bae wako ndi bae chabe Kwa ma hope anga amagulisa zibwente Broz yake imakonda ma cartoon a ben 10 Ndikafuna ku chiller Ndimatenga dollar ya zibwente Ndi chilichonxe cha Ben 10 Ndikatelo am in skueeww Kudya kudya kudya kundya kudya Zibwente(Turn up)×4 Ndigotenga hanz Ndikagonama ngat ndikufuna zibwente Kenako ndipange chimasamu kuti man Ka Chick nditenge Ine ndi mfana wa chabe Kasitomala wa masten ake Best friend wa broz yake Ndimagolowa ndiya zibwente Amake a Lisa Ndikufuna zibwente Ngat chenje chikuvuta Masten Mumuuze Lisa atenge Kwa ma hope anga amagulisa zibwente Broz yake imakonda ma cartoon a ben 10 Ndikafuna ku chiller Ndimatenga dollar ya zibwente Ndi chilichonxe cha Ben 10 Ndikatelo am in skueeww Kudya kudya kudya kundya kudya Zibwente(Turn up)×4 Malawi Kudya zibwente za ten Za twenty thirty Za fifty Ndi watch yokha ya Ben 10 Broz yake singalimbe She was like clispy u feel this Coz u crazy G Nanga zigenge za twenty Za thirty zomwez Mpaka kumwela tea Ndamuthoka kuti Ndine captain bae Bae wako ndi bae chabe Ndine captain bae Bae wako ndi bae chabe Kwa ma hope anga amagulisa zibwente Broz yake imakonda ma cartoon a ben 10 Ndikafuna ku chiller Ndimatenga dollar ya zibwente Ndi chilichonxe cha Ben 10 Ndikatelo am in skueeww Kudya kudya kudya kundya kudya Zibwente(Turn up)×4
Lyrics powered by www.musixmatch.com
Get up to 2 months free of Apple Music
instagramSharePathic_arrow_out