Lyrics

MMMH (Njuchi) Chibwenzi si banja Kulephera sikugonja One Ndamva zoti amaku player Ukafusa amakumenya Mpaka zafika chonchi Akuti amaku Yuza Kwa anzake ndiwe nzake Ukumakakamira But lady you are beautiful Mani ndinu handsome Alipo winawake samagona tulo Mukangomuyankha moni Zitaye Zitaye Mwaiwe muli bandulo You are better off without him Zitaye Zitaye Mwaiwe muli bandulo Bandulo Two You are better off without him Mami (Mami) Ntendele ndi ufulu mami (Mami) Never let him fool you Love is just a word So many wanna use you mami Mutaye Mutaye Bwera betchi ngati sungampeze Wina woposera iyeyo Auntie phodani Ngati uli dolo phusha harder Uncle Lowani gym Muzipatse nthawi Muzitolere muwale Azigwidwa manyazi Eeeh Anzake onse atsikeni Zithunzi zake dilitani Asakupusitseni mu blockenii Put up a smile mami zijambuleni Yeah Anzake onse atsikeni Zithunzi zake dilitani Asakupusitseni mu Blockenii Put up a smile mami tengani Selfie Zitaye Zitaye Mwaiwe muli bandulo You are better off without him Zitaye Zitaye Mwaiwe muli bandulo Bandulo Zitaye Zitaye Mwaiwe muli bandulo You are better off without him Zitaye Zitaye Mwaiwe muli bandulo Bandulo
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out