Lyrics

Mic check Mic check One two, one two Ase wayamba ku recorder Aaa ok tiyeni tiyambe Mtima ukapuma Zichewa pakamwa Mudzi nawo umasungulumwa Tinali naye dzulo Tadya naye nkhomalilo Oh ndatopa m'masomu tulo Tiwonana mawa ndikaone pillow Sindikudziwa chidzanditenge ndichani Chonde musadzalile inu Mzimu wanga udzadzadzidwa ndichimwemwe Musazadandaule Awuzeni alowe Andione nkhope komaliza Akamaliza andipelekeze Malo a zii wo Awuzeni alowe andione nkophe komaliza Andipelekeze, (ine ine) Malo a zi wo Aay ndidzakhala pompo ndili mu form ya mzimu Ndidzidzaona chilichonse Osaopa sindizaona zinazo Timiseche sindidzamva nawo Adzukulu adzakusana makasu mammawa mwina Azimayi masana adzayimba hosanna Malo a zi timukonzele mudzi Anyamata tikumbe pati Apo ayi pali miyala Apa bwino pali a uje Akapume akatchole batcha ndi mbalame Kanali ka n'yamata kokonda nthabwala Auzeni anambe kumphikako njala, (aaa ntchito timadyela ka) Nde ndidzidzangoseka Malo a zi wo Mu uzimu ndidzasuzumila kumphika Malo a zi wo Anambe akutsinkha ndiwo Malo a zi wo Ena mwa mwayi adzapeza banja Mmm yeah malo a zi wo (malo a zi wo) Malo a zi wo (malo a zi wo) Malo a zi wo (malo a zi wo) Malo a zi wo (malo a zi wo) Ndidzamva wizulo amayi amvano Oh kani ndimkakondedwa chonchi (malawilano) Mayambililo tapanga chimvano Mukamadzalila ndidzasisima Dzalitonthozeni kholo langa Azibale anga, azinzanga
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out