Lyrics

Machesi Ndayatsa but you're already on fire Moto obadwa nawo amakutcha born fire Nkhani ndi nkhani kodi zimatheka bwanji Nditenge madzi mwina nkudzandi tentha Kodi mayi, mayi! Mayi waona ndani? Mayi ukumwa chani? Mayi dzina ndi ndani? Kodi mayi, mayi! Mayi waona ndani? Mayi ukumwa chani? Mayi dzina ndi ndani? Ali bububu! Nkazi ali bububu! Lit nga chigubububu Chance ili ukuku ili ukuku Size yangatu Maine gwileni ndingafe Nkazi mikanda ili mbwee Chiwuno chofewa ngati bread Ali diku diku ali peng yeah! Ali Peng yeh! Ngati bread yeh! Akufewa yeah Diku diku yeh! Diku diku yeh! Diku diku yeh! Diku diku yeh!
Writer(s): Teddy Maliza Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out