Listen to Get There (feat. Maskal) by Gwamba

Get There (feat. Maskal)

Gwamba

Hip-Hop/Rap

547 Shazams

Lyrics

Everytime you're feeling down Everytime you're feeling weak Yang'ana kumwamba you'll get there Everytime you're feeling down Everytime you're feeling weak Yang'ana kumwamba you'll get there You'll get there, you'll get there Yang'ana kumwamba you'll get there Yeah, aish Pena ngati mwina ndingogivah Ndikupemphera koma mbuye sakundimva Njala, nthenda, mavuto andiliza Ndikuwona ngati mwina bible limatinamiza Zitseko zamadalitso ndayesa ku knocker Mbuye sakutsegula padakali poloka Ndikulakwitsa pati? Mwina ndikakwere phiri Ndiwuzeni zochita, mavutowa ndi ambiri Mafunso achuluka koma palibe oyankha Nde m'malo molira timadzukabe nkukankha Mtima ukuwawa ife timasekelera Timadziwa tsiku lina madalitso adzatigwera, yes Everytime you're feeling down Everytime you're feeling weak Yang'ana kumwamba you'll get there Everytime you're feeling down Everytime you're feeling weak Yang'ana kumwamba you'll get there You'll get there, you'll get there Yang'ana kumwamba you'll get there Aish, anakupatsa mimba nkuyikana Usowa chochita poti udakali mwana Kukanika kugona, usiku kumangolira Dekha, ambuye Yesu adzakupatsa njira Unalemba mayenso osakhonza? Lembanso Kumenya hustle osatheka, menyanso Osagivah iwe simfana wa weak Ngati pano sizutheka yesa kumenyanso repeat Kuli mavuto odetsa nkhawa Usalire yang'ana za mawa Everytime you're feeling down Everytime you're feeling weak Yang'ana kumwamba you'll get there Everytime you're feeling down Everytime you're feeling weak Yang'ana kumwamba you'll get there You'll get there, you'll get there Yang'ana kumwamba you'll get there Everytime you're feeling down Everytime you're feeling weak Yang'ana kumwamba you'll get there Everytime you're feeling down Everytime you're feeling weak Yang'ana kumwamba you'll get there You'll get there, you'll get there Yang'ana kumwamba you'll get there You'll get there, you'll get there Yang'ana kumwamba you'll get there
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out