Lyrics

"Time Waits for no one" papa told me So don't waste it darling Umoyo wanga ni olimbikila Nika ganiza kwamene nachokela Mutima uma pwanya Sinifuna kubwelela Ndiye chifukwa nima yesa Koma siniziba Nthawi zina chima lema Koma siniziba Nthawi zina sini maziba Nika yan'gana bonse ba nzanga Nina yamba nabo Nima ganiza kapena ni taya nthawi Vonse nima yesa Vonse nima chita Kapena sini chita vokwanila Koma amai akuti Mwana wanga vonse vili na nthawi Uku kuyesa kwamene uyesa pano Siku taya nthawi upunzila Koma siniziba Nthawi zina nima lema Koma siniziba Nthawi zina sini maziba Siniziba kulimba Siniziba vochita Siniziba voganiza Ndine muntu chabe Ni malema koma osa leka Uzafika Baliko bamene sibenzo ziba Nthawi zina Bana fika Nawe uza fika
Writer(s): Enala Zyambo Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out