Lyrics

Mtima wanga umaimba Everytime I see your face ka ngelo weh Love yanga sizasila Sili monga kendulo You make my heart go like duduke Every time you see me Moteromo mmene umandikondela Nikumveka mendulo I don't need no special day To make you feel you special Poti kwa iwe ndi ine Everyday is valentines Umanipasa mtendere, mtendere, mtendere eh Umani mvesa chimwemwe changa ndiwe Umanipasa mtendere, mtendere, mtendere eh Umani mvesa chimwemwe changa ndiwe Nditu baby you are my piece of mind Mmani pangiso deka Ambiri ama kaikira alole adziwe Ndita kala wanje Koma ndiwe nyenyezi yanga Omwe azabwera mowala Ncholinga ndisatire You make me sing skubi dubi doo Skubi dubi dubi doo Dubi like the way I do Saza mwalile Umanipasa mtendere, mtendere, mtendere eh Umani mvesa chimwemwe changa ndiwe Umanipasa mtendere, mtendere, mtendere eh Umani mvesa chimwemwe changa ndiwe I don't wanna lose you I don't wanna hurt you, no I just wanna see you smilling (I just wanna see you smiling) Ndiwe mtendere wanga Chimwemwe changa ndiwe Zonse zanga ziimbila iwe Umanipasa mtendere, mtendere, mtendere eh Umani mvesa chimwemwe changa ndiwe Umanipasa mtendere, mtendere, mtendere eh Umaninvesa chimwemwe changa ndiwe, yeah (Umanipasa mtendere, mtendere, mtendere eh) (Umani mvesa chimwemwe changa ndiwe) (Umanipasa mtendere, mtendere, mtendere eh) (Umaninvesa chimwemwe changa ndiwe, yeah)
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out