Featured In

Credits

COMPOSITION & LYRICS
Yobe Gweula Phiri
Yobe Gweula Phiri
Songwriter
PRODUCTION & ENGINEERING
Ace-Tee
Ace-Tee
Producer
Madela
Madela
Mastering Engineer
Patrick Tsoka
Patrick Tsoka
Creative Director
Emmah Msiska
Emmah Msiska
Creative Director
Lisungu L-Static Phiri
Lisungu L-Static Phiri
Creative Director

Lyrics

Classic Ace-Tee on the beat Eyo mayne Wasup bruh Who is this Jesus you keep rapping about, mayne Ndi ndani kwenikweni aise Alright, so you wanna know Him Yeah, mayne Okay, listen Za Iye unazimvapo kale Koma sumazitengera umangoti zikhale Zimakumvekera mwa nthano, no wonder you doubt it Mtima unawuumitsa, you don't wanna be about it Eeh! I relate 'cause nane n'nali choncho Before the Truth hit my heart n'nali Bonzo And religion made it worse, inali smoko N'kona ndinkadzimva u atheist ngati dolo Komano n'takumana naye man Amene ndin'kati ndi myth Maso anatseguka ndinati ndimutsate man Truth is who I'm rolling with Nde pano palibe angandinamize adha Zi philosophies of men sizingandihite adha Got the Living Word in me, sentence singafike adha Olo atandijaja, bola I truly know Him adha Dziko limam'kana koma silimadziwa man Silimadziwa man Kuti Iye si munthu wamba Ndi Namalenga samafera opinions of man Opinions of man Ndipo siudzamva 'Cause Iye ndi Madradra, dradra Dradra, dradra And enawa ndi ma blunter, blunter Blunter, blunter Let's go deeper now I'm just being a vessel, the Spirit is your teacher now Ngati golden hour, you gonna have the picture now Of who Christ really is mpaka umudziwa nawo Yeah! Ey, Iye n'Namalenga He's uncreated nde creation imalenga And He sustains us ndi zomwe amanena Ndi mwa Iye yekha momwe ife tipeza worth bruh Nde zija unamva zoti anadzatifera man Ndi zoona, sikuti n'zongopeka man Koma it's a reality kwa tinadzipereka man Moona, He became our Savior man And we were made partakers of His sacrifice Moti tinafa naye, n'kuuka naye m'mandamo N'kugonjetsa adani onse ndi chi landslide Palibiletu angapange raise madando Dziko limam'kana koma silimadziwa man Silimadziwa man Kuti Iye si munthu wamba Ndi Namalenga samafera opinions of man Opinions of man Ndipo siudzamva 'Cause Iye ndi Madradra, dradra Dradra, dradra And enawa ndi ma blunter, blunter Blunter, blunter Yeah, that's it mayne. And just because man denies the deity of Jesus Christ it doesn't Mean kuti He stops being God, nah He is God and He doesn't depend on man's opinion about Him. Man has to know that Jesus is supreme in power, glory, authority and importance Ndi Madradra Yeah, Yobezani Ndi Madradra Ace-Tee on the beat
Writer(s): Yobe Phiri Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out