Lyrics

Ah Hee Ah Hee Ah Hee Yeah hee Mukukamba zinkhani zambiri Mukufuna ndiwononge mbiri Kodi nchikondi Ndimayesa tilimo awiri Muli ndi nthawi muli busy Chonde msachimwise Ayi nsadanise Ndi wangayu Achuluka anthu okhomelela ahahaha Kankhani pang'ono kupemelela koma why ATI ndingofuna ndingokudyela ineyo Atumapo anthu kuzandikwenya ndee Tinamenyana Mumvetse Olo mu dameje dameje Kumuleka sizingatheke Ndimadana ndi mtopola Muleke Zomakamuwuza miseche Ndicholinga choti athese Ndimadana ndi mtopola Ine ndimadana ndi mtopola Mtopola eh mtopola Mtopola eh mtopola Ndimadana ndi mtopola Ndati ndimadana ndi mtopola Mtopola eh mtopola Mtopola eh mtopola Ndimadana ndi mtopola Yeah Umaganiza bwanji kukwatira beast Iweyo ndi Ka beauty ofunika Prince Mamuna Oti nthumba anathila yeast Osati kafinyanya wonunkha gilisi Mhuu koma mtopola Ndizamumveso wina nzamunokola Kumawuza anzake andisomphola Ndizamponda pamutu ndi chigogoda Cell nzalowa Bola ndamtchola Eya pezani zina zochita Eya kupeza wanu nzovuta Eya mungomupempha Chauta Osativuta Mwachuluka anthu okhomelela Kankhani pang'ono kupemelela ATI ndingofuna ndingomudyela Koma tizamenyana Mumvetse Olo mu dameje dameje Kumuleka sizingatheke Ndimadana ndi mtopola Muleke Zomakamuwuza miseche Ndicholinga choti athese Ndimadana ndi mtopola Ine ndimadana ndi mtopola Mtopola eh mtopola Mtopola eh mtopola Ndimadana ndi mtopola Ndati ndimadana ndi mtopola Mtopola eh mtopola Mtopola eh mtopola Ndimadana ndi mtopola Olo mu dameje dameje Kumuleka sizingatheke Olo mumuwuze miseche Yeah ey yeah Yeah ey yeah Ndimadana ndi mtopola Mtopola eh mtopola Mtopola eh mtopola Ndimadana ndi mtopola Ndati ndimadana ndi mtopola Mtopola eh mtopola Mtopola eh mtopola Ndimadana ndi mtopola Mtopola eh mtopola Mtopola eh mtopola Ndimadana ndi mtopola Mtopola eh mtopola Mtopola eh mtopola Ndimadana ndi mtopola
Writer(s): Joy Gondwe Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out