Listen to Ndifunsa (feat. Skeffa Chimoto & Joe Kellz) by Macelba

Ndifunsa (feat. Skeffa Chimoto & Joe Kellz)

Macelba

Hip-Hop/Rap

1,732 Shazams

Lyrics

Uuuuuh Ooh ooh! Look Dear admin Dzulo ndinagona osaphaka Sungandimvetse admin yeah Dzana nali ndimafriends timayaka Nkawauza ndudutsamo sandimvetsa Bola nzingothokoza kuti anandimwetsa Nine months pano ngini yanga yangoima Ka hope kanga nkakango'no Zizayenda mwina Koma admin eh Paden rent yanga njosasotha Kupha nyerenyere anzanga akugula ma motha Zingongole mbwee ndigwire mtengo wanji Koma zikundivuta bwanji Ndikatchena ngati ndilibe mavuto (mayoh!!) Pandekha kusisima ndazazidwa ndimavuto Am looking for an answer Zikatere mumatani Mundifunsire kugulu but please hide my ID Mtima nde kufuna ufuna Kufunsa nzeru Kwa anzanga ndi abale Ndikudutsa muzambiri ine Pandekha sinkwanitsa no Komano nkhawa bii ine Nkutheka ndinyozeka But I will say it anyway so please Hide my ID Ndifunsa Ndifunsa ndifunsabe But please Hide My ID Ine mungondithandiza so please Hide my ID Ndikufuna nzeru zanuzo Osati chitonzo chanucho ooh! Yah Dear admin Ndili osweka mtima Sindikumvetsa admin Kapena vuto ndine mwina Ndikayesera kukonda zimangothera misonzi Nazilakwira chani mphongozi Mesa mmati zizakhala better Kapena nalengedwa kuzafa mbeta Wanga mamuna amveka bwanji mphete wina Wanga mamuna wapereka pathupi kwina Pressure ya anzanga afuna tonse tikwatire Pressure ya amama zizukulu akumbatile Ndikaphoda ngati ndilibe mavuto Pandekha kusisima ndazizidwa ndi mavuto Am looking for an answer zikatele munatani mundifunsire kugulu But please hide my ID Mtima nde kufuna ufuna Kufunsa nzeru Kwa anzanga ndi abale Ndikudutsa muzambiri ine Pandekha sinkwanitsa no Komano nkhawa bii ine Nkutheka ndinyozeka But I will say it anyway so please Hide my ID Ndifunsa Ndifunsa ndifunsabe But please Hide My ID Ine mungondithandiza so please Hide my ID Ndikufuna nzeru zanuzo Osati chitonzo chanucho Nkhawa njeee Osadanda dzina ndiye sititchula Koma yankho lenileni komanso lowona Ndiye ndi ambuye basi You've got a role to play Muli ndi mbali yoti muchite Ngati munthu muyanga'ne M'mene muchitira zinthu zanu Mwina mukumachita komabe Pena osachita bwinobwino Mwina kumasamba thupili Mtima uli waumve zedi Kutheka kumakankhadi zoona Koma osadziwa komwe ukukankhila You've got to balance Muziwunguze Mukachita mbali yanu Kwinako timsiyire ambuyee Hide my ID Ndifunsa Ndifunsa ndifunsabe But please Hide My ID Ine mungondithandiza so please Hide my ID Ndikufuna nzeru zanuzo Osati chitonzo chanucho
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out