Lyrics

Na-na-na, Namadingo, oh Sooner or later somebody is gonna say it, eh Just a matter of time, yeah Koma they'll surely say it, say it Kapena mwina ndinene Ndinene ndine 'Cause somebody has to I see a lot of my sisters across the world on social media Shaking it, kuligwedeza Even on a picture sangangoyima bwinobwino Koma atembenuke, anthu awone telera Brother Dan ndiwokwatira koma Instagram sagona tulo Brother Manzy sakupuma Scrolling down and zooming in, awone telera Alongo ena akumadziva kupelewera Mpaka kusaka m'mankhwala abaye nawonso zitheke Zili kuma WhatsApp status Akumati happy customer Kubaya kamodzo, mwezi umodzi, telera yabwera Koma si galimoto lili lonse lifunika telera Designer ku factory ndimomwe adali konzera Musatsutsane ndi designer, sizimankondwetsa Corolla adapanga kuti no-no-no telera Mira no, no-no-no telera Demio no telera Isiyeni truck, it's okay, telera Koma benz no, no-no-no telera Beamer no-no-no, no-no, no-no-no telera Isiyeni flat liner ikoke telera Osatsutsana ndi designer No-no-no telera
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out