Lyrics

This is ionine Soldier, Lucius Banda Standing shoulder to shoulder With Coss Chiwalo Back home Ufalitsi ndi wokhometsa misonkho Adapita kukapemphera Adalikunga pemphero mfalitsi Lodzitamandila pamaso pa Yahweh Wokhometsa nsonkho adangoyima Paka corner kudzimvela chisoni Pemphero lake lidali lalifupi Ambuye khululukireni ochimwa ine Tagundika tuthandiza wosowa Komatu ndiye zachifalitsi Katundu wake okwana mu jumbo Koma pa social media photo mbwe mbwe mbwe Amanyoza omwe achita zanzeru Akuti iwo ndiye abwino Sadziwa anzawo atsatira malemba Chaku manja chakumanzere chisaone Tikadzitchula kuti ndife abwino Tidzinyenga chabe Tikadziona ndife alunga-lunga Tingopusa chabe Poti wabwino ndi Mulungu yekha Wosachimwa kose Mavuto onse tipereke kwa iye Iye wotilenga Ndikuti palibe Palibe munthu wopanda tchimo Dziko lapansi ndi lochimwa Adatitsoka mtunda, madzi Woyipayo atsikira konko Oh palibe Palibe alibe mavuto Ali wa moyo pa dziko lapansi Oh ndi iyeyo Ndiyekhayo womwalira Wathana nazo zapadziko Muli nchisimu choweluza Awa ngoyina inu ngabwino Mumayiwala munthu aliyense Ali ndi zake zofooka Aliyense pa dziko pano Ali ndi mtanda wake womuzunza Awo ndi chamba, awo ndi mowa Awa kunyenga, awa ngotolatola Tikadzitchula kuti ndife abwino Tidzinyenga chabe Tikadziona ndife alunga-lunga Tingopusa chabe Poti wabwino ndi Mulungu yekha Wosachimwa kose Mavuto onse tipereke kwa iye Mbuye wotilenga Palibe munthu wopanda tchimo Dziko lapansi ndi lochimwa Adatitsoka mtunda, madzi Woyipayo atsikira konko Palibe alibe mavuto Ali wa moyo pa dziko lapansi Ndiyekhayo womwalira Wathana nazo zapadziko Pali kagulu ka anthu ena Amakonda kunyogodola Akawona nzawo akuvutika Samathandiza awo m'manong'onong'o Aliyense padzikopa inu Ali ndi nthenda yomwe idzamuzunze Ena ndi sugar, BP, asthma Khunyu, edzi ena adzalumala Tikadzitchula kuti ndife abwino Tidzinyenga chabe Tikadziona ndife alunga-lunga Tingopusa chabe Poti wabwino ndi Mulungu yekha Wosachimwa kose Mavuto onse tipereke kwa iye Mbuye wotilenga Palibe munthu wopanda tchimo Dziko lapansi ndi lochimwa Adatitsoka mtunda, madzi Woyipayo atsikira konko Palibe alibe mavuto Ali wa moyo pa dziko lapansi Ndiyekhayo womwalira Wathana nazo zapadziko Palibe munthu wopanda tchimo Dziko lapansi ndi lochimwa Adatitsoka mtunda, madzi Woyipayo atsikira konko Oh palibe, palibe alibe mavuto Ali wa moyo pa dziko lapansi Oh ndi iyeyo Ndiyekhayo womwalira Wathana nazo zapadziko Palibe munthu wopanda tchimo Dziko lapansi ndi lochimwa Adatitsoka mtunda, madzi Woyipayo atsikira konko Palibe alibe mavuto (Ali wa moyo pa dziko lapansi) (Ndiyekhayo womwalira)
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out