Lyrics

One genius tings (hey) Mmh Hey honey it's a good morning madzi ndatenthetsa Koma musanakambe Happy ndili m'mafuso atatu Kodi nkhope yangayi yokongola m'mayichemelerayi Nditati ndapanga zilonda kumaso konse mungandikonsenso? Shape yangayi ya coca cola m'mayisapotelayi Nditati ndawonda ngati nthiko honey mungasapotenso? Sitepe yangayi m'mati ndimayenda ngati odziwa mwayi Zitati ulumari wandigwera mungalabadenso? Mankhwala a moyo ndi passion Ine kukhulupilira nthawi tamvera As we breathe usapeze chifukwa chondikondera Koma passion ndi kulimbikira honey tamve-era As we breathe usapeze chifukwa chondikondera Moyowu pena sungatheke Mayeso pena sangaphweke Bwanji uzikonzekeletse Kundikondabe in any ways Moyowu pena sungatheke Mayeso pena sangaphweke Bwanji uzikonzekeletse Kundikondabe in any ways In any ways In any ways I know ukaona ka passo munsewu umasilira ndikumapanga compare Honey ali ndi kabaza, mu jumbo ndi ngumbi madzulo akabwela Koma ndikulangize it's only a humble beginning Baby mupilire, kunyanja m'malota uli mu bikini Udzagula Fortuner yachi engine chopuma Udzavala zodula, ma saloon otukuka (ih yeah) Mankhwala a moyo ndi passion Ine kukhulupilira nthawi tamvera As we breathe usapeze chifukwa chondikondera Koma passion ndi kulimbikira honey tamve-era As we breathe usapeze chifukwa chondikondera Moyowu pena sungatheke Mayeso pena sangaphweke Bwanji uzikonzekeletse Kundikondabe in any ways Moyowu pena sungatheke Mayeso pena sangaphweke Bwanji uzikonzekeletse Kundikondabe in any ways Oh-weh, oh-weh, oh-weh, oh-wah Oh-weh, oh-weh usandikondele looks honey Oh-weh, oh-weh Oh-weh, oh-weh, oh-weh, oh-wah Oh-weh, oh-weh usandikondele chuma honey Oh-weh, oh-wah, oh-weh, oh-weh Oh-weh, oh-wah, (ay yeah) Mankhwala a moyo ndi passion Ine kukhulupilira nthawi tamvera As we breathe usapeze chifukwa chondikondera Koma passion ndi kulimbikira honey tamve-era As we breathe usapeze chifukwa chondikondera Moyowu pena sungatheke Mayeso pena sangaphweke Bwanji uzikonzekeletse Kundikondabe in any ways Moyowu pena sungatheke Mayeso pena sangaphweke Bwanji uzikonzekeletse Kundikondabe in any ways (matama aja adah)
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out