Lyrics

Udzindimvera udzindimvera pena Udzindimvera udzindimvera baby Udzindimvera udzindimvera pena Udzindimvera udzindimvera baby Palibe muthu amadziwa zonse Zayekha anavika nsima madzi Kuyenda awiri simatha Zodziwa iwe nane singadziwe Kulipo kumafa ndiludzu Kulipo kumanka kutali Kumakafufuza zeru katali Okondeka wanga ndifunse Ndidalile okondeka wanga Ndiyang'ane okendeka wanga Ndidalile okondeka wanga Nditha kukhala opanda Ndalama Koma undidali okondeka wanga Undiyang'ane okondeka wanga Udzindimvera udzindimvera pena Udzindimvera udzindimvera baby Udzindimvera udzindmivera pena Udzindimvera udzindimvera baby Ngati nkutukuka tidzatukuka tonse Ku shayina ku shayina tonse Udzindimvera udzindimvera baby Dzatuka dzatuka tonse Ku shayina ku shayina tonse Udzindimvera udzindimvera baby Usadzadziwe ntapita kale Usazadzadziwe ine atanditenga Mwendo wanga unali madzi Nanga bwanji ndimafa ndi ludzu Pena ndimavetsa kukula kwako Tasiyana ndife a chimodzi Koma ukadziyi lemekeza ndalama Udzandisiya pa dzuwa Ndidalile okondeka wanga Ndiyang'ane okendeka wanga Ndidalile okondeka wanga Nditha kukhala opanda Ndalama Koma undidali okondeka wanga Undiyang'ane okondeka wanga Udzindimvera udzindimvera pena Udzindimvera udzindimvera baby Udzindimvera udzindmivera pena Udzindimvera udzindimvera baby Ngati nkutukuka tidzatukuka tonse Ku shayina ku shayina tonse Udzindimvera udzindimvera baby Dzatuka dzatuka tonse Ku shayina ku shayina tonse Udzindimvera udzindimvera baby
Writer(s): Lawrence Khwisa Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out