Listen to Fumbi (feat. Eli Njuchi) by Gwamba

Fumbi (feat. Eli Njuchi)

Gwamba

Hip-Hop/Rap

Lyrics

Treaky beats ooh ooh Kuyambila 25 mpaka 49 Kwa Gona Kwa cent kunchesi mpaka Biwi Koseko amandikonda Mfana wa 25 wam'Dubai kwa Gona Kwa cent kunchesi mpaka Biwi Koseko amandikonda Ndikangofika mubwila fumbi Kuno ndikwathu amandikonda Ndikatela mubwila fumbi kuno ndikwathu amandikonda Ndikafika mubwila fumbi kwathu amandikonda Njuchi ikatela mubwila fumbi kwathu amandikonda Too much love ngati kuli show Mbizo alikomko Akangoyimba ndekuti yathela pompo Mafana onse omwe anabela style Ndiyamba kulipilitsa nsonkho Kuyamba 1,8 chapa Chester Pano golf club ija timakhometsa Anthu kudabwa eeh ambilife school njee Nanga bwanji machongetsa Ndikavaya BT ndix Ndili pamtima pawo vix Ndikalowa Zuze chiwavi Mafana akundikanganila ngati mjavi Ndikangofika mubwila fumbi Kuno ndikwathu amandikonda Ndikatela mubwila fumbi kuno ndikwathu amandikonda Ndikafika mubwila fumbi kwathu amandikonda Njuchi ikatela mubwila fumbi kwathu amandikonda Too much love No am not lucky am blessed Sikuthekela Kwa ine ndi grace Pano ndikafika kumakhala fumbi Koma sungalisese Osabwela kuzasiya minyama Ukaphweketsa ghetto mphwanga, uwona kiyama Tikakuona Ukupanga zosiyana Nafeso tinafightila Chakufwa Chihana Nchani nayamba tili mwana pano Tikuwala ngati ndine kendulo whoah Yehova kundikweza mwamba ndimkadya Otambalala pano ndipatebulo Iwe ndikangofika mubwila fumbi Kuno ndikwathu amandikonda Ndikatela mubwila fumbi kuno ndikwathu amandikonda Ndikafika mubwila fumbi, kwathu amandikonda Njuchi ikatela mubwila fumbi, kwathu amandikonda Kuyambila 25 mpaka 49 Kwa Gona Kwa cent kunchesi mpaka Biwi Koseko amandikonda Mfana wa 25 wa m'Dubai kwa Gona Kwa cent kunchesi mpaka Biwi Koseko amandikonda
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out