Top Songs By Crispy Malawi
Similar Songs
Credits
PERFORMING ARTISTS
Crispy Malawi
Performer
COMPOSITION & LYRICS
Chifundo Chingaipe
Composer
PRODUCTION & ENGINEERING
Cheo Meek
Mixing Engineer
Lyrics
Pomwe Pali Bho-Po ifeso tili pompo (Ifeso tili pompo) (Pompo)
Koma komwe kwavaya gulu lakolo
Suzatipeza konko (Sungatipeze konko) (Konko)
Ndili pa easy sinduyaka
Ndangodekha ndungosipper Coco (Ndungosipper Coco) (Coco)
Koma utha ku trappa Baby Gin
Alembe bill yanga pompo (Pa Bill yanga pompo) (Iwe) Olo
Olo Fanta utha ku trappa fukwa si ine Malinga
Ndine Spe-Malawi mfana wama dinkamu
Ndili njapa koma undipeza m'tikamu (Uh huh)
Zisangalalo zodanda ndazitsika
(Huh, Huh, Huh)
Sizimachitika chitika koma leroli zachitika (Hee, Hee, Hee)
Kufewa, kufewa, kufewa ine si Swazi wa Chipika
Weekend ndimashala Stu koma lero ndili outside ku chiller ndima mandem
Take me back to the old days tikuyakakira Mbowe, Gazebo ndipa Game
Homeboy amawoneka panza koma atha kukhala oyamba kuthawa pa ndeu
Rest in peace to Martse Nkhata lero tigona panja, party ili pa nseu
Bed ndi tulo mkati ife tigona panja (Lero tigona panja)
Ndingofuna good vibes only, bad energy panja (Bad energy panja)
Girls just wanna have fun, boys ingofuna zaza (Boys ingofuna Zaza)
Ma babe anu Sali safe, boys yanga ili outside
From Mzuzu to the Bay, mad victions and the lake[?]
Pa denga and the lake, underrated, underpaid
Outdated all these fakes, now it's money over sex
Koma Thako tagwedeza, ndiziponya cash ineyo (Ineyo)
Ndiyathu ija, kukonda chills Ndine June, Mpasha yama Ninja
Tingoplaya tima tune, yatsa Zaza ija
Ndili chaku moon ndi Hunny wachi figure
Koma ndi singer, andisoka mwina (Mwina)
Kubwera sober pamalo tayakitsa (Tayakitsa)
Tili panja ndi boys ya inside (Inside)
Yang'anitsitsa iyi ndi street fight (Fight), ndi zima peace sign
Monalisaaaa, (Yeah)
Monalisaaaa, (Yeah)
Weekend ndimashala Stu koma lero ndili outside ku chiller ndima mandem
Take me back to the old days tikuyakakira Mbowe, Gazebo ndipa Game
Homeboy amawoneka panza koma atha kukhala oyamba kuthawa pa ndeu
Rest in peace to Martse Nkhata lero tigona panja, party ili pa nseu
Bed ndi tulo mkati ife tigona panja (Lero tigona panja)
Ndingofuna good vibes only, bad energy panja (Bad energy panja)
Girls just wanna have fun, boys ingofuna zaza (Boys ingofuna Zaza)
Ma Babe anu Sali safe, boys yanga ili (Ayy) (Ayy) (Ayy) outside
Ndi boys tikuchiller Ka, Ku blues tingofila Ka
Olimbana nafe ali m'madzi tikumwa Miller Ka
Spe Wapota Reefer ka, uku ndikusipper Ka
Mfana wodelera wakumana nayo Inkata
We livin' a soft life but we go harder with these punches
I'm with the homies mahn so know sometimes we get rachet
And leave you in some crutches
Koma tayima Kaye tikuchiller ase
These ladies just want me to tap fukwa ndiku dripper Ase
Ndinafika Ase nde kenako ndinapita ase Ndikuballer opanda keeper Ase
Zi bhawa tikungothila Ase
Spiced up ngati Rajah tadya Zaza Ase, Meek kweza speaker Ase
Weekend sitiyambilatu Friday, utipeza Thursday man tikungofila aire
Saturday ndili pa easy ndili ndi boys tikuwupeza
Mafana oyera Mtima koma tikumana pa Zodetsa eish!
Weekend ndimashala Stu koma lero ndili outside ku chiller ndima mandem
Take me back to the old days tikuyakakira Mbowe, Gazebo ndipa Game
Homeboy amawoneka panza koma atha kukhala oyamba kuthawa pa ndeu
Rest in peace to Martse Nkhata lero tigona panja, party ili pa nseu
Bed ndi tulo mkati ife tigona panja (Lero tigona panja)
Ndingofuna good vibes only, bad energy panja (Bad energy panja)
Girls just wanna have fun, boys ingofuna zaza (Boys ingofuna Zaza)
Ma Babe anu Sali safe, boys yanga ili outside
Cheo Meek Hihihihi Hihihihi
Lyrics powered by www.musixmatch.com