Lyrics

Pamtima panga panadza lumpha ndikamva walowa mumpanda, Walowa munyimba ndimunthu wanga uyu Inde ndi banja komanso munthuyu ndimzanga (munthuyu ndimzanga) Pali iyeyo kuseka tsiku shota ngati pali iyeyo (pali iyeyo) Pali iyeyo ndimadzidabwa ndekha ngati pali iyeyo mwa ifeyo Muli mijedu mijedu ndife chi bank cha nkhani Mijedu mijedu ndife chi bank cha tinkhani muli mijedu Mije Mije(kuseka tsiku shota ngati pali iyeyo) mije(pali iyeyo) Tilindi kujeda a neighbor ndi anzawo tinawaseka Tilindi kujeda tizibwenzi ta anzake tasekedwa Nde tikamaseka mpaka misonzi m'masomu Nde tikamaseka mpaka nthiti kuwawa Pali iyeyo kuseka tsiku shota ngati pali iyeyo (pali iyeyo) Pali iyeyo ndimadzidabwa ndekha ngati pali iyeyo Mwa ifeyo muli mijedu mijedu ndife chi bank cha khani Mijedu mijedu ndife chi bank cha tinkhani Mijedu
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out