Lyrics

Yeah yeah yeah yeah yeah Yeah yeah yeah yeah yeah Yeah yeah yeah yeah yeah yeaaah yeah yeah Yeah yeah yeah yeah yeah Yeah yeah yeah yeah yeah yeaaah TrickyBeatz Kalikokha nkanyama Mtima wanga wasankha iwe Ndilole ndikukonde Ndilole ndikukonde ndikukonde Kalikokha nkanyama Maso anga aona iwe Ndizotheka ndikukonde? Nzotheka ndikukonde? Nyumba ikulilenji Nsima ya munthu mmodzi koma ikusala Chakudya sichikoma Ndimangotaya Maka mdima ukagwa Mkati mwangamu umadzala nkhawa Ndikazampeza sazandithawa ine Mwina zachikondi zinandilaka ine Tsano Chikati gogogo chili pa iwe chili pa ine Chili pa iwe chili Ngati ngumbi londo londo Komwe upite ndikusatile Komwe upite ndikusatile shuwa Gogogo chili pa iwe chili pa ine Chili pa iwe chili pa ine Ngati ngumbi Komwe upite ndikusatile eh Kalikokha nkanyama Mtima wanga wasankha iwe Ndilole ndikukonde Ndilole ndikukonde ndikukonde Kalikokha nkanyama Maso anga aona iwe Ndizotheka ndikukonde? Nzotheka ndikukonde? Zanga zonse tenga ndakupasa Mtimau unalasa iwe dale wanga Iwe Dale wanga Chilichonse tenga ndakupasa Mtima unalasa iwe Dale wanga Iwe dale wanga Tsano chikati gogogo chili Pa iwe chili pa ine Chili pa Iwe chili Ngati ngumbi londo londo Komwe upite ndikusatile Komwe upite ndikusatile shuwa Gogogo chili pa Iwe chili pa ine Ngati ngumbi komwe upite ndikusatile Eh Kalikokha nkanyama Mtima wanga wasankha Iwe ndilole ndikukonde Ndilole ndikukonde Ndikukonde Kalikokha nkanyama Maso anga aona iwe Ndizotheka ndikukonde? Nzotheka ndikukonde? Kalikokha nkanyama Mtima wanga wasankha Iwe ndilole ndikukonde Ndilole ndikukonde Ndikukonde Kalikokha nkanyama Maso anga aona iwe Ndizotheka ndikukonde? Nzotheka ndikukonde?
Writer(s): Chifuniro Kasiya Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out