Listen to MADA (Remix) [feat. Ace Jizzy, Bee Jay, K Banton, Waxy Kay, Guntolah, Che Kalonda, Mellz Kumpanje, Jeg & Jolasto] by Phyzix

MADA (Remix) [feat. Ace Jizzy, Bee Jay, K Banton, Waxy Kay, Guntolah, Che Kalonda, Mellz Kumpanje, Jeg & Jolasto]

Phyzix

Hip-Hop/Rap

207 Shazams

Lyrics

Yeah It's Only Entertainment Cuff-B Production Sameface on the Beats Mumakwana a Mada Mwabhebha mwabhebha Mwaipatsa moto a Mada Mwatentha mwatentha Woozzah Akakhosomola ndekuti afuna pizza Amadaliso nthumba mwawo sachedwa ku pisa Issa mpaka namupangisila Viza Nkazi oti nangokumana naye pa Instagram Pano ndi mlamu Mmhu am so dam Ine nkangofuna kudya Buble gum hmmm Murder Murder Murder Murder hmm satha kumvetaa Pena Gena zomwe imapanga the other gender Pakakhala Dollar imangobenda Yeah Malo mopala moto undipalimulisa Mabomba a rasha ndizindikila nda phulitsa Katundu wanuyo ndikuziwa mumagulisa Mdulidwe wazimayi kulibe nde osadulisa Iiih aMada Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Iyiyi nde ndi Murder Case Murder Case Murder Case Iyiyi nde ndi Murder Case Murder Case Murder Case Zofuna za Mada ase Zikangolowa ku madance eti Kugula Gin Wawa Castel Aphula sin akangotell Mhuu Uyu singagwire mwa easy Kundipasa chance singasinze Ngati chux ndi maplan ndili busy Kuti ukhale mula wa Jizzy Nkazi wachi body chonyadisa Nde sinzakubisa anthu akudziwe Pa Facebook, Insta ndi Twitter Ndikasintha picture pakakhala iwe Koma MADA doesn't care Ena ATI ndika wash and wear Ndimamufuna kuposa mpweya Mundilangiza ine Osamvera aaah Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Iyiyi nde ndi Murder Case Murder Case Murder Case Iyiyi nde ndi Murder Case Murder Case Murder Case Ukumachita kundigwedezera matako mada Ine si charisma pa Tuno Aaah FADA (alipo samafuna kudya) (mada) ine ndiofewa mchiuno Atandimanga sangamve zokuti Umachita kundipeza wekha kwathu kuno Nde panopa sukumavalamo mwado (mada) Ukumangongoyenda buno buno Ndikati easy umati NO Umaipatsa moto (ipondeni fadah) Umaiwala zoti amanjata (Gwii) Ufuna ndikalowe ndi Mada Why you gotta do me like this mada Ukufuna kuti ndipange commit mada Ukupanga chani madalitso Ufuna khoba izawatenge fada Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Iyiyi nde ndi Murder Case Murder Case Murder Case Iyiyi nde ndi Murder Case Murder Case Murder Case Mpaka ndiphula ma sin kamba ka iwe Mada Wina ndimuNYIKA ndimadana ndizaFANTA Ndakumvela kuwawa kuti ufike apapa Ndipo muwuzane wina ndimuchotsa mphafa Unaponya status ukumenya nip Sikuti ndikuku kumba ndangowona ma pic Kuyiwala kwanu unapanga mistake Ati Blantyre sinodi? Zawu wayilesi Madaaa kaya unafa kwambiri Nane ndi mfumu ndikudyesa ma tick Ukuwonjeza my queen Nane town ndiyanga ngati maskin Eti uli blues? Ukumwa manica? Ukuspendar dollar uli ndi ma nigga? Eti zafika poti boys ikukugwila? Ati uli ready akufunayo aika? Mada mbuyo monsemu sinakhale case Mwina ndili mwana kusewelesa zikhesi Koma anthu akwathu akati napangidwa curse Akazi ndinkagwila ngat Shammah no reverse Nkaz opanda mbuyo Kumandibwenza mmbuyo Sinaphake naye life ati Anali smoke sinatchaye olo life Ati Samva Maloza Chifukwa chan anaonapo maloza Ati x wake sankapanga cholozeka Asing'anga agwila ntchito ine ndekha ndolozeka Koma inalipo nthawi yosowa chochitika Ma Beat mangonyika Asilamu akudanda ati sindipanganika Kubwera mada kuwelama Kuzasikana kenako kukwerana Ndichi red sign nkona tikufilana. MADA Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Iyiyi nde ndi Murder Case Murder Case Murder Case Iyiyi nde ndi Murder Case Murder Case Murder Case Mwana kazi undipweteka Unditakasa Undipepeta Ndikagona Ndiku Mbrupahur hvd Ndiku bwebweta! Upange zomwe wanena Ndipo ndizione zikuthekeka Ngati wati cheke Cheke apa! Ndikuone ukuchekeka iiiyh MADAm mada ukalola Ine wadya!! MADA undimadalits Iii taonani undibalalitsa! Azimayi Nthungululu pamenepa! Amanena kuti love Is blind Ine kuno khungu Nde yandipweteka Sindikuona komaso sindikubona undivetse Dzina ndani? Madalitso Ndiwe okongola ngati ku paradizo Tabwera kuno mdzataniso? Tiime pachulu ngati bwana Mbizzo Ana okuposa palibetu Or nkhalamba paliJETU Gaire ndalama pa Easy'tu Dollar yaine sungamalizetu Ine ndi mponda matik Ndimamenya mponda ma kick Nkonda ma gig nkonda ma chick Mada usanditole tola ma pic Umulore MADA gangster Honey moon ndiku MADA gascar Ndamva zoti wakana chi namtindi Iwe ndiine love Mwantinti Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Iyiyi nde ndi Murder Case Murder Case Murder Case Iyiyi nde ndi Murder Case Murder Case Murder Case Mfana ophulitsa life ngati Makombola Kuthamanga kwambiri kuposa Corolla Kumuuza Kuti tiye amangolola Chilichonse atha kupanga nabola Dolla Nde Ali Ndi chi figure Ngati Masamu Dzimatatoo Mbwee Mmatakomu Wapengetsa Ma Bwana Ntaunimu Koma Chonde Usadye Ndi Halamu Nde Mwati iyeyu ndi Ndani (KAYA) Wabwera Ndi Ndani, Akumwa Chani (KAYA) Mwina Kapena Ndimupatse Plan Mmmmh Dadda Uyu Akuchedwetsani Akazi akalowa mu boy zone Olimbana nao amwa poison Bambo anga paza kuden zima weapon Wina azakushoshe azalira Ring tone Iwe Uzangomva ngiri ngiri Wina azanditenge kuchigwiri gwiri Amuna anga alusiratu kuno dada Amuna anga atha kupalamula mada Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Iyiyi nde ndi Murder Case Murder Case Murder Case Iyiyi nde ndi Murder Case Murder Case Murder Case Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Mwanakazi Mwanakazi Undipalamulitsa Iyiyi nde ndi Murder Case Murder Case Murder Case Iyiyi nde ndi Murder Case Murder Case Murder Case
Writer(s): Noel Phyzix Chikoleka Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out