Lyrics

Baby Love ya bwanji iyi Ndikamakhala pena Osamvetsetsai How do we connect How do we make sense How did we meet Ih yeah ih yeah Anthu awiri from different worlds Koma zochita kuchita limodzi Anthu ochoka different worlds Mtima kugunda kugunda pamodzi Chikondi ichi ichi Sindimachimvetsabe eti Love iyi iyi Sindimayimvetsabe eti Love iyiyi Chikondi ichichi Love iyiyi Chikondi ichichi You know seh gangster Ndayesetsa kukhala stable Kudzigwira komabe I'm not able Eti ine kuthawawa Kubisabisa Kuzembazemba Osafuna kuonetsera Kuti ndazelezeka nawe baby Wandimalizitsamo eti Yey yey mmm yeah You're like kokaina You get me higher inna Love Love yeah Chikondi ichi ichi Sindimachimvetsabe eti Love iyi iyi Sindimayimvetsabe eti Love iyiyi Chikondi ichichi Love iyiyi Chikondi ichichi Pena we do think we don't deserve love mmm Everybody needs love (Needs love) Everybody deserves to be loved (Deserves to be loved) He my kokaina He gets me higher inna In love love yeah Chikondi ichi ichi Sindimachimvetsabe eti (No no no) Love iyi iyi Sindimayimvetsabe eti (No no no) Love iyiyi Chikondi ichichi Love iyiyi Chikondi ichichi This love This love yeah Love iyiyi Chikondi ichichi (Chikondi ichichi) Love iyiyi (This love yeah) Chikondi ichichi mmmm
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out