Music Video

Featured In

Credits

PERFORMING ARTISTS
Faith DJ
Faith DJ
Rap
samuel!
samuel!
Background Vocals
COMPOSITION & LYRICS
Angella Faith Montfaucon
Angella Faith Montfaucon
Songwriter
PRODUCTION & ENGINEERING
samuel!
samuel!
Producer
Trust Msowoya
Trust Msowoya
Producer
Essim and Animal Lab Production
Essim and Animal Lab Production
Video Producer
Matthew Mphande
Matthew Mphande
Producer
Yesaya Nkhwazi
Yesaya Nkhwazi
Producer

Lyrics

Moyo umatibwetsela zambiri Zina zotiwawa zina za Chisoni kwambili Sizimatengela pomwe ife tili Kapena kuti ndikoyamba kaya kachiwili Koma Yesu atikondabe kwambili Amakhala kuti watitchinjizira ku zambili Kumbukila mawu ake akuti Chikhulipililo chimasuntha mapili Mu chikondi chake mantha alibe malo Ndikudziwa ukumva ngati uli pa chibalo kude bwanji dzula libwera mmalo Usiku uli ndi malile, satana alibe malo Mu chikondi chake mantha alibe malo Ndikudziwa ukumva ngati uli pa chibalo kude bwanji dzula libwera mmalo Usiku uli ndi malile, satana alibe malo Tonthola usalile chifukwa Kwa Iye ndiwe chifukwa Usataye mtima chifukwa Moyo wako uli ndi chifukwa Nditonthola ine Chifukwa Kwa Iye ndine chifukwa Sinditaya mtima chifukwa Moyo wanga uli ndi chifukwa Nthawi zina sitimamvetsa Ambuye ndi chani chikuchitika Zimangokhala ngati alipo Akufuna titafinyika Koma kumbukilani mawu anena Mdani wanthu si munthu ogwilika Moyowutu ndi muuzimu Ndipo padziko pano sindifetu mzika Pukuta misonzi leza mtima Chonde usataye mtima Khulupila ndikuchita mawu Ake Siumila, suwotcheka, moyo wako ndi wake Pukuta misonzi leza mtima Chonde usataye mtima Khulupila ndikuchita mawu Ake Siumila, suwotcheka, moyo wako ndi wake Tonthola usalile chifukwa Kwa Iye ndiwe chifukwa Usataye mtima chifukwa Moyo wako uli ndi chifukwa Nditonthola ine Chifukwa Kwa Iye ndine chifukwa Sinditaya mtima chifukwa Moyo wanga uli ndi chifukwa Tipilize kupemphela Tipitilize kudekha yep Tipilize kuchenjela Tipitilize kukhulupilila Imva izi Nyimbo y'a chiyembekezo Imva izi Nyimbo y'a chitinthozo Imva izi mawuwa ndichenjezo Maganizo oyipawo Usamve zimenezo Chita mbali yako Mulunguso achita mbali Yake Yesi anabwela ndi mpulumutsi wako Ndiwe opambana maso Ake Chita mbali yako Mulunguso achita mbali Yake Yesi anabwela ndi mpulumutsi wako Ndiwe opambana maso Ake Tonthola usalile chifukwa Kwa Iye ndiwe chifukwa Usataye mtima chifukwa Moyo wako uli ndi chifukwa Nditonthola ine Chifukwa Kwa Iye ndine chifukwa Sinditaya mtima chifukwa Moyo wanga uli ndi chifukwa Tonthola usalile chifukwa Kwa Iye ndiwe chifukwa Usataye mtima chifukwa Moyo wako uli ndi chifukwa Nditonthola ine Chifukwa Kwa Iye ndine chifukwa Sinditaya mtima chifukwa Moyo wanga uli ndi chifukwa
Writer(s): Angella Montfaucon Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out