Lyrics

Oh-oh ooh udah dey I don't wanna lose you And I'll never leave you Baby baby Baby baby The way you hold me When you tell me how much you miss me I don't wanna lose you That's why I choose you The way you hold me When you tell me how much you miss me I don't wanna lose you That's why I choose you Ine ndimakukonda (Zoona) Kuchoka pansi pa mtima (Zoona) Mushe I'll never leave you (Zoona Zoona Zoona) Nane ndimakukonda (Zoona) Kuchoka pansi pa mtima (Zoona) Baby I'll never leave you (Zoona Zoona Zoona) Monga momwe mayi amakondela mwana Chikondi chako pa ineyo ndichokwana Ayi osadzadana izi sizachibwana Momwe ndawonela ifeyo tagwirizana Ndendende drug ndi chipatala Iwe ndi ine sitidzasiyana Uwawuze akapasule Iwе ndine mpakana muyaya The way you hold me Whеn you tell me how much you miss me I don't wanna lose you That's why I choose you The way you hold me When you tell me how much you miss me I don't wanna lose you That's why I choose you Ine ndimakukonda (Zoona) Kuchoka pansi pa mtima (Zoona) Mushe I'll never leave you (Zoona Zoona Zoona) Nane ndimakukonda (Zoona) Kuchoka pansi pa mtima (Zoona) Baby I'll never leave you (Zoona Zoona Zoona) Ukadzandisiya I'll lose my mind (lose my mind) Ukadzandithawa I'll lose my mind (lose my mind) Koma m'mene m'makukondela ngakuthawe babe (oh no) Even if you lose your mind ine ndzayitolera Ine ndimakukonda (Zoona) Kuchoka pansi pa mtima (Zoona) Mushe I'll never leave you (Zoona Zoona Zoona) Nane ndimakukonda (Zoona) Kuchoka pansi pa mtima (Zoona) Baby I'll never leave you (Zoona Zoona Zoona) The way you hold me When you tell me how much you miss me I don't wanna lose you That's why I choose you The way you hold me When you tell me how much you miss me I don't wanna lose you That's why I choose you Ine ndimakukonda (Zoona) Kuchoka pansi pa mtima (Zoona) Mushe I'll never leave you (Zoona Zoona Zoona) Nane ndimakukonda (Zoona) Kuchoka pansi pa mtima (Zoona) Baby I'll never leave you (Zoona Zoona Zoona)
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out