Lyrics

Iwe ndi Ine (iya-na-na-na-yoh) Yah man (Iwe ndi Ine) This is ionine soldier Lucius Banda And the ras in it Standing shoulder to shoulder With Dan Lu wachiyawo wangalusa Atinena sitikhalana Cholinga chawo tiziyambana Tisiyane apeze danga Pachoka nzako pali malo Ati chikondi chathu sichingalimbe eh Ndipo sichamuyaya Mphuno salota Inu wake Ife mpaka kumanda Onena zinenani Oseka zisekani Onyoza zinyozani Okwiya zikwiyani, ooh yeah Ife taponda mwala Ndipo sitikayika ngati pali ena munachedwa Iwe ndi Ine mpaka kale Iwe ndi Ine mpaka kale (kavalidwe Iwe mkakusamala) Iwe ndi Ine (Iye) mpaka kale (poti ndiwe wakunsana) Iwe ndi Ine mpaka kale Mumkatilembera malire Sangathe two months Kenako yapita five years Kenako phaa ten years Takhala limodzi dzaka zonsezi Akhala akukamba zambirimbiri Mwakhala mukuponya ma spy in our love life But here we are Iye ndi ine eeh, tikasiyane eeh Chomwe Ambuye adalitsa no man can put a sender Iye ndi ine eeh, tikasiyane eeh Chomwe Ambuye adalitsa no man can put a sender Iwe ndi Ine mpaka kale Iwe ndi Ine mpaka kale (kavalidwe Iwe mkakusamala) Iwe ndi Ine (Iye) mpaka kale (poti ndiwe wakunsana) Iwe ndi Ine mpaka kale Posiyana pano panatidutsa Polekana panapitilira Ndife thupi limodzipalibe chomwe mungachite Mudzingoyang'ana (Iye ndi Ine) muzingosilira Potilekanitsa panadutsa we just want nobody Iwe ndi Ine mpaka kale Iwe ndi Ine mpaka kale (kavalidwe Iwe mkakusamala) Iwe ndi Ine (Iye) mpaka kale (poti ndiwe wakunsana) Iwe ndi Ine mpaka kale (mmh) Iwe ndi Ine (na-na-na-na) mpaka kale Iwe ndi Ine mpaka kale (kavalidwe Iwe mkakusamala) Iwe ndi Ine (Iye) mpaka kale (poti ndiwe wakunsana) Iwe ndi Ine mpaka kale Iwe ndi Ine mpaka kale Iwe ndi Ine mpaka kale Wayimanya wayimanya
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out