Lyrics

Nanana namadingo Oo Nana ooonana I have been here be izi zimandiopsa Where I remember this thing ndiverera mantha Falling in love ndi mtima onse eeh But in return cheating on me kundinamiza aah aah Ndinkakanika kugona all night talking to Myself kumazifunsa ndikupererewera pati? Ine zimenezo ayiiiii Nkhani yachikondi Khani ya chikooondii Nkhani ya chikondi Ine ndikufuna ndizinva sugar Nkhani ya chikondi Nkhani ya chikooondii Nkhani ya chikondi Ine ndikufuna ndizinva sugar Babe Zachi zachi zachikondi(sugar) Babe zachizachikondi(sugar) Babe zachikondi (bring me sugar) Na na Nana nanana namadingo yeah When I keep myself to love there is no holding back yeah No looking back mmh mmmh Old time I got you back but when you lose me I'm never coming back Chifukwa ine ndimazipereka ah kuja kotheratu Ukandisiya ngati mtimawu susweka for sure ung'ambika Sindimafuna kuzanva phuma ngati mwinandiphulika I don't want that love I just want sweet love For the Bible says umukonde mnzako momwe uzikondera mwini Nkhani ya chikondi Nkhani ya chikooondii Nkhani ya chikondi Ine ndikufuna ndizinva sugar Nkhani ya chikondi Nkhani ya chikooondii Nkhani ya chikondi Ine ndikufuna ndizinva sugar Nkhani ya chikondi Story yachikoondiii Nkhani ya chikondi Ine ndifunache kufiling'a sugar Kufiling'a sugar Sugar Bring me sugar Nanana Nana namadingo
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out