Lyrics

You already know (Tricky Beats, ooh, ooh) Loved you for a long long time You've been mine for a long long time Kwathu unadzawonekeranso But in my dreams zonsezi In my dreams I love you but I can't say I want you but I can't say I need you but I can't say Poti uli ndi wako kale Wa ndalama kale Ali ndi chi thilakitale Komanso ndimawopa ine Vuto ndine singakwanitse lobola Vuto ndine singakwanitse lobola Kandalama kanga ndikochepa Singakwanitse lobola Kandalama kanga ndikochepa Singakwanitse lobola Is it true what they say? Mkazi okongola Malawi yonse Ndimbali zinayi zaku UK Atinso USA, oh-ah Anaku controller Anukugulilanso mortal love Singakwanitse olo Motorola Komabe umandidolola I love you but I can't say I want you but I can't say I need you but I can't say Koma nalota utandilola Koma lobola inandibalalitsa m'maloto mwanga Vuto ndine singakwanitse lobola Vuto ndine singakwanitse lobola Kandalama kanga ndikochepa Singakwanitse lobola Kandalama kanga ndikochepa Singakwanitse lobola In my life you comе first like Genesis My first lovе like a diamond, yeah I love you but I can't have you Mthumba mwanga m'mopanda malo Oh, ndimakukonda koma ndalama ndilibe Oh, ndimakufila koma singakukwanitse Vuto ndine singakwanitse lobola Vuto ndine singakwanitse lobola Kandalama kanga ndikochepa Singakwanitse lobola Kandalama kanga ndikochepa Singakwanitse lobola
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out