Lyrics

Wachibale ndiwe m'bale Wangawanga ndiwe wachibale ndiwe m'bale Wachibale ndiwe m'bale Wangawanga ndiwe wachibale ndiwe m'bale Sindinawone munthu wolimba mtima ngati iwe wachibale (Ndiwe m'bale) Sindinawone munthu wokonda mzake ngati iwe wachibale (Ndiwe m'bale) Tinakumana ku secondary kalero Umbwanawewo unayamba ndi kalero Blood is thicker, thicker than water But do remember water is life Wina ubale umabadwa moyenda Mu ntauni muno timalerana abwanawe Wachibale ndiwe m'bale Wangawanga ndiwe wachibale ndiwe m'bale Wachibale ndiwe m'bale Wangawanga ndiwe wachibale ndiwe m'bale Sindinawone munthu wolimba mtima ngati iwe wachibale (Ndiwe m'bale) Sindinawone munthu wokonda mzake ngati iwe wachibale (Ndiwe m'bale) Ndinali ndi ondilonda ochuluka anandithawa Zikatha ndalama umandigaila ndikundigailanso mbalume Ponda apa mponde Ukasuntha ndifutepo, atha kutitapa phanzi Gwira chanza bwanawe Mtima wanga wakufwanthulira njota, landira ulemu wako Wachibale ndiwe m'bale Wangawanga ndiwe wachibale ndiwe m'bale Wachibale ndiwe m'bale Wangawanga ndiwe wachibale ndiwe m'bale Sindinawone munthu wolimba mtima ngati iwe wachibale (Ndiwe m'bale) Sindinawone munthu wokonda mzake ngati iwe wachibale (Ndiwe m'bale)
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out