Lyrics

Kwawachera pa bwalo onena miseche Inu muli kalikali mpakana zitheke Akusintha ma shift kujeda M'mawa mpaka madzulo Nkuda ali m'magulu mpaka m'bandakucha Kujeda (mpakana kuche) Mayi wanga (mpakana zitheke) (Mapeto ake), ayimba cha? (Ayimba wizulo) (mpakana kuche) Mayi wanga (amayi mpakana zifewe) (Mapeto ake), ayimba cha? (Ayimba wizulo) Muwaleke okonda zopingana Adzingowona mutalandira madalitso Muwaleke okonda zolondana Adzingowona mutalandira madalitso Kumati ndiye chokondwetsa ndi chani pano? Muzakuvutika kwanga, mpaka pa bwalo Chosonkhanila ndikuti mundijede basi Koma mangani malamba muchezera pano Anthu oyipa inu Mpakana kuche Mpakana zitheke Mapeto ake ayimba wizulo Muwaleke okonda zopingana Adzingowona mutalandira madalitso Muwaleke okonda zolondana Adzingowona mutalandira madalitso Onani Nyerere zipanga ma bwalo kugwirizana zotuta (zituta) Zituta ndi khama usiku mpaka m'bandakucha Kodi inu monga munthu mumatani? Nanga mwapindula chani ndikunenana? Mpakana kuche Mpakana zitheke Mapeto ake ayimba wizulo Mpakana kuche Amayi mpakana zifewe Mapeto ake ayimba wizulo Muwaleke okonda zopingana Adzingowona mutalandira madalitso Muwaleke...
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out