Lyrics

I worried all the time I thought I'm running out of time Can't take it a day at a time sometimes Man our dreams have been too loud since We were only young kids And now, we grown they loud still I know ndizambiri umafuna mtima Nde pena mantha ankadzandigwila Like what if we don't make it [yeah yeah What if we don't make it Koma tachoka nkutali Mulungu anali ndi pulani Pulani Inu Zonse ndi nthawi Mulungu anali ndi pulani Pulani Yopanga za ifeyo [oooh oooh oooh Yopanga za ifeyo Akupanga za ifeyo [oooh oooh oooh Akupanga za ifeyo Yoh Venue yomweyo ena amaflopa Samatrenda nyimbo zawo akadropa Nde pena pride imafuna idzindikopa Koma mbuye wanga sangakondwe kuti nzizipopa Nde rule number 1, kumakhala humble Poti ukazikweza amasiya kupanga zako Rule number 2, osakhala ndi tsankho Poti lero ndi kape mawa ali pamwamba pako Nkayang'ana kumbuyo ngati ndingokuwa mbuye Ndinakhonza chani kuti inu mundimasule Mwandichotsa kutali kwinakunso Mulambule Ulendowu ndiwautali koma Koma tachoka nkutali Mulungu anali ndi pulani Pulani Inu Zonse ndi nthawi Mulungu anali ndi pulani Pulani Yopanga za ifeyo [oooh oooh oooh Yopanga za ifeyo Akupanga za ifeyo [oooh oooh oooh Akupanga za ifeyo
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out