Lyrics

Yoh yoh yoh yeah Mmmh mmmmh Yachina Yeah yeah Undipeza pa home ground san silo Ubweletse ganja aise five kilo Ndima liva soft life five pillows Maluzi kuno nde tikuwachinya five zero Mfana olimbikila hustle ngati maskini Pakhomo zingati aise? five pini Mafana kuyesa ngati mwina ndima user khini Ma babe ndungogwila ma bomba Charles Swini Kuspenda money ngati mwana wa politician Money laugh haha ndikugiligishani Phone yanga osaimba palibepo mission Iye nde dancehall ina ija tiku deletitsani Oii ndili bwino muli bwa? Tikumwela kuno inu muli kwa? Pa bwandilo tinapitilapo nyama Zakathela short time ndi bwa? Pasapezeke fanta pa bill yanga No iyi si bill yanga Ndavala tinted ayesa Steve Wonder Mowa wina ukutanipo pa bill yanga Bartender noo iyi si bill yanga Noo iyi si bill yanga Mkazi uyo yekha amwa pa bill yanga Ana akenso adzakhala pa will yanga Ma style ambiri mbiri Hot like piri piri Two two three three Black beema Kukumveka dancehall ko ndikomwe ife tili Ndine chair wa zinginizi who? Bakili kili Genna wa droppa ina Ona zima Babe zikuvina Pa Bill yanga vunga nso round ina Amafuna abele style ndasintha kuika ina Ndakumana ndichichi mwana Phuli Phuli Chondipatsa nkhuli nkhuli Chimafila dancehall ndichipatsa phuli phuli Rich like Muli Muli Muli bwa? muli uli? Weh we deh yachina hehehe fully fully Ukandipeza pa Zode Tsaa Ndili ndi achina Mode Staar Amafuna glass ndampatsa ya Gin I didn't know kuti amafuna aphode Pasapezeke fanta pa bill yanga No iyi si bill yanga Ndavala tinted ayesa Steve Wonder Mowa wina ukutanipo pa bill yanga Bartender noo iyi si bill yanga Noo iyi si bill yanga Mkazi uyo yekha amwa pa bill yanga Ana akenso adzakhala pa will yanga Pasapezeke fanta pa bill yanga No iyi si bill yanga Ndavala tinted ayesa Steve Wonder Mowa wina ukutanipo pa bill yanga Bartender noo iyi si bill yanga Noo iyi si bill yanga Mkazi uyo yekha amwa pa bill yanga Ana akenso adzakhala pa will yanga Yeah Yeah Yachina, Fully! You know how di ting go my G Weh we deh Ife ndi mafumu like Makanjira Ku spenda money Mpinganjira Ndikafika likkle bwoy sintha njira Big dawg yow puppy bwoy pinda nchila Weh we deh
Writer(s): Chikumbutso Banda Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out