Lyrics

Ndili ndimafuso oti sindingakwanitse kuwayankha Poti mayankho ake ali kuseli kwa moyo Abambo anga ndimafuna mtawaonaso ali ndi moyo Pena mtima umalirabe mukakumbukira malemu, amayi anu Makolo ena amalira akakumbukira mwana wawo, adatsogola ah-ah Ena tikulakalaka one time Titangokumanaso ndima best friends Inde malemba! ati kuli moyo wina Wamuyaya kumwambako Koma ngati ndi zotheka Tikamadzapita akatichingamire Tikamadzapita akatichingamire, otidziwa Tikamadzapita akatichingamire abale athu Tikamadzapita akatichingamire, ey For we know we've been missing you We've been missing yeah I miss my father, oh Abambo anga ndawasowa Somebody misses somebody, oh Malemba apitiliza kufotokozapo za moyo wina Ati kulibe ubale, ukwati ku moyo wina Mpamene adadi ndimawakumbukira Kuwaganizira, pena ndimalira, ay Mpamene agogo ndimadwawaona Atavala corona wawo Pi-di-di-di die, mafunso mumtima, ah-ah Wopanda mayankho Kodi ndine ndekha amene ndili ndi mafuso opanda mayankho? Kodi mayankho anga ali kuseli kwa moyo Ndani sadalakelakepo atangomuonaso winawake ali ndi moyo? Tikamadzapita akatichingamire Tikamadzapita akatichingamire Tikamadzapita akatichingamire abale athu Tikamadzapita tikaonanenso ndi abale athu For we know we've been missing yeah We've been missing yeah Oh, oh, yeah I miss my father, oh, oh Somebody misses somebody now, yeah Abale athu tawasowa Tikamadzapita ah, ah Tikamadzapita ah, ah-ah (sha gramos) Akatichingamire, eeh, eeh-ehe Blessings been with righteous people Fire upon my wicked people This has been my walk from Africa to the Caribbeans Let every man and every woman Lift your voice to the top of the Mount Zion For the most high to see our tribulation In their condition to the redemption We give thanks and praise for the salvation Respect to the one and only Almighty God Jehovah Ti-ti-ti-ti, tikamadzakwela mudzatichingamire Tikamadzabwela mudzatichingamire Na-na-na-na-na, Namadingo oh, oh
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out