Lyrics

M'mati chani kodi ma guy? Koma anthu enawa (mmh mhu) From the ghetto to the rasta bwoy tings yeah (aah) Ey, sindimanyuma ine mantha njee Mutu ndinayika kale panjanje Mfana wamuthewera pamper njee Mumampopayo pa ine sanganjanje Sindimanyuma ine mantha njee Mutu ndinayika kale panjanje Mfana wamuthewera pamper njee Mumampopayo pa ine sanganjanje Yeah, kuwawa ndinasiya kumva Sungamuvetse pain Ras anagontha N'nakumana nazo n'nazidutsa Palibe chachilendo ungandichite, kumbutsa Me burn fire are weh turn your eye red (phu-phu) Hater wanga sangafile iry di (fire) Still man I win my bread You can't do me dirty like mid dread, bwoy Sindimanyuma ine mantha njee Mutu ndinayika kale panjanje Mfana wamuthewera pamper njee Mumampopayo pa ine sanganjanje Sindimanyuma ine mantha njee Mutu ndinayika kale panjanje Mfana wamuthewera pamper njee Mumampopayo pa ine sanganjanje Usamasuke ngati nsalu palibe chomwe ungachite (njee) Kukhuta therere kusapangitse zako zide-njee Shosha yadzukulu udzikumbile wekha dze-nje Ndinamva mandimu mphwanga osati malala-nje Kude kuche man ah struggle and suffer real out here Sinditchena m'mangobisa malise-shiii Eya ndine mwana okula opanda mache-za Sindimanyuma ine mantha njee Mutu ndinayika kale panjanje Mfana wamuthewera pamper njee Mumampopayo pa ine sanganjanje Sindimanyuma ine mantha njee Mutu ndinayika kale panjanje Mfana wamuthewera pamper njee Mumampopayo pa ine sanganjanje Sunganditolele n'nabwela kuzabwembwezela Ma hater kundipeza ine kuwapezelera Sindiganiza zobwelera sine osochera N'nabwera kudzakhala komano moyimilira Ilakwe ilakwe game zikwanje Sindimanyumwa sindichita manjenje Iyi ndi ya umkano ya usimba ulenje Ukaphweketsa ndikuonjezera bwenje Sindimanyuma ine mantha njee Mutu ndinayika kale panjanje Mfana wamuthewera pamper njee Mumampopayo pa ine sanganjanje Sindimanyuma ine mantha njee Mutu ndinayika kale panjanje Mfana wamuthewera pamper njee Mumampopayo ooh! yeah Sindimanyumwa ine pamper njee (aaah) Sindimanyumwa mantha njee! (out)
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out