Top Songs By Chizmo Sting
Similar Songs
Credits
PERFORMING ARTISTS
Chizmo Sting
Performer
COMPOSITION & LYRICS
Chizmo Sting
Composer
Lyrics
M'mati chani kodi ma guy?
Koma anthu enawa (mmh mhu)
From the ghetto to the rasta bwoy tings yeah (aah)
Ey, sindimanyuma ine mantha njee
Mutu ndinayika kale panjanje
Mfana wamuthewera pamper njee
Mumampopayo pa ine sanganjanje
Sindimanyuma ine mantha njee
Mutu ndinayika kale panjanje
Mfana wamuthewera pamper njee
Mumampopayo pa ine sanganjanje
Yeah, kuwawa ndinasiya kumva
Sungamuvetse pain Ras anagontha
N'nakumana nazo n'nazidutsa
Palibe chachilendo ungandichite, kumbutsa
Me burn fire are weh turn your eye red (phu-phu)
Hater wanga sangafile iry di (fire)
Still man I win my bread
You can't do me dirty like mid dread, bwoy
Sindimanyuma ine mantha njee
Mutu ndinayika kale panjanje
Mfana wamuthewera pamper njee
Mumampopayo pa ine sanganjanje
Sindimanyuma ine mantha njee
Mutu ndinayika kale panjanje
Mfana wamuthewera pamper njee
Mumampopayo pa ine sanganjanje
Usamasuke ngati nsalu palibe chomwe ungachite (njee)
Kukhuta therere kusapangitse zako zide-njee
Shosha yadzukulu udzikumbile wekha dze-nje
Ndinamva mandimu mphwanga osati malala-nje
Kude kuche man ah struggle and suffer real out here
Sinditchena m'mangobisa malise-shiii
Eya ndine mwana okula opanda mache-za
Sindimanyuma ine mantha njee
Mutu ndinayika kale panjanje
Mfana wamuthewera pamper njee
Mumampopayo pa ine sanganjanje
Sindimanyuma ine mantha njee
Mutu ndinayika kale panjanje
Mfana wamuthewera pamper njee
Mumampopayo pa ine sanganjanje
Sunganditolele n'nabwela kuzabwembwezela
Ma hater kundipeza ine kuwapezelera
Sindiganiza zobwelera sine osochera
N'nabwera kudzakhala komano moyimilira
Ilakwe ilakwe game zikwanje
Sindimanyumwa sindichita manjenje
Iyi ndi ya umkano ya usimba ulenje
Ukaphweketsa ndikuonjezera bwenje
Sindimanyuma ine mantha njee
Mutu ndinayika kale panjanje
Mfana wamuthewera pamper njee
Mumampopayo pa ine sanganjanje
Sindimanyuma ine mantha njee
Mutu ndinayika kale panjanje
Mfana wamuthewera pamper njee
Mumampopayo ooh! yeah
Sindimanyumwa ine pamper njee (aaah)
Sindimanyumwa mantha njee! (out)
Lyrics powered by www.musixmatch.com