Lyrics

Butter It's butter baby yah Ah huh Allegik, Allegik, Allegik Allegik, Allegik, Allegik Ukatalikila ndi mavutika ineyo Ukangosutha ndi mabanika, ah Mutu sumagwila, mutu sumakoka Zoti ndi dealer pa town zosamveka Mutu sumagwila, Mutu samakoka Zoti Ndi Doba pa town zosamveka Ngati Ali juju munanditha baby G-Sali stable pano ndi teke teke Gelo asachoke ineyo gwede gwede Pitikoti government, mpheche peche Ngati Ali juju munanditha baby G-Sali stable pano ndi teke teke Gelo asachoke ineyo gwede gwede Pitikoti government, mpheche peche Allegik, Allegik, Allegik, yah Allegik, Allegik, Allegik, yah Sindifuna wina komano Iweyo Sindifuna pena, Komatu pa iweyo Sindifuna wina komano Iweyo Sindifuna pena, Komatu pa iweyo Allegik, Allegik, Allegik, yah Allegik, Allegik, Allegik, yah Sindifuna wina komano Iweyo Sindifuna pena, Komatu pa iweyo Sindifuna wina komano Iweyo Sindifuna pena, Komatu pa iweyo Ma group mu akuti ineyo ndapenga Mental disorder yapa zombayi ndaposa Ndili busy ine ndi vama love Azinzanga samabwela kwanthu I don't know what you did to me Mami don't stop me coz I like it I don't know what you giving me Ipatse moto Mamie coz I want it Ngati Ali juju munanditha baby G-Sali stable pano ndi teke teke Gelo Asa choke ineyo gwede gwede Pitikoti government, mpheche peche Ngati Ali juju munanditha baby G-Sali stable pano ndi teke teke Gelo asachoke ineyo gwede gwede Pitikoti government, mpheche peche Allegik, Allegik, Allegik, yah I'm Allegik welewoh Allegik, Allegik, Allegik, yah I'm Allegik Sindifuna wina komano Iweyo Sindifuna pena, Komatu pa iweyo Sindifuna wina komano Iweyo Sindifuna pena, Komatu pa iweyo Allegik, Allegik, Allegik, yah I'm Allegik welewoh Allegik, Allegik, Allegik, yah I'm Allegik Sindifuna wina komano Iweyo Sindifuna pena, Komatu pa iweyo Sindifuna wina komano Iweyo Sindifuna pena, Komatu pa iweyo
Writer(s): Armstrong Sopani Kalua, Sunday Godwin Joshua Lyrics powered by www.musixmatch.com
Get up to 2 months free of Apple Music
instagramSharePathic_arrow_out