Lyrics

Ooooh, mmmmhhh Mmh Sunkati ndinali kale Lero wandifuna iwe galu eti Zikupeta unkati mphale Lero tikudya iwe usale Ngongole unkati sunday, monday kenako Usandipatse Pano ndikuchakacha nde uzindipempha iwe ndi bakha eti Ndinjoye nane Ndiyibakisheleko nane Ndikutapa ngati wa ndale Hi Ho Zi ma ho ngati Vicky Marley Iwe Sungayimake Size singakukwane Unayiphwekesa kale mpake sukutukuka nawo m'bale Ndinakuuza kale Karma izakutsata Karma izakutsata Karma izakutsata Karma izakutsata Zoma eh khomelelana ndi za chimwana Zoma pangilana nsanje ndi za ku nkaka Zoma eh khomelelana ndi za chimwana Zoma pangilana nsanje ndi za ku nkaka Nditakufusila unandikana Lero (hey baby), iwe gwape eti (aaah) Iwe ndikatchula honey Imakhala money, mukawuzane Amanditcha bwana KingPin (Shasha) Ndimacheza ndi ma ding ding ding Ndikumveka ngati ringing Nde uzindifuna are you kidding me? ah Sungayimake Size singakukwane Unayiphwekesa kale mpake sukutukuka nawo m'bale Ndinakuuza kale Karma izakutsata Karma izakutsata Karma izakutsata Karma izakutsata Zoma eh khomelelana ndi za chimwana Zoma pangilana nsanje ndi za ku nkaka Zoma eh khomelelana ndi za chimwana Zoma pangilana nsanje ndi za ku nkaka
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out