Lyrics

Tiye tiyambe Aye aye yeah Aye aye Nawe umandiyimilila ndikakhala pansi Umandichotsa ludzu ndikafuna madzi Ndiwe sindidzasowa kanthu Eish kunyadilana, kunyadilana Kupatsilana chimwemwe mosawuzana Kudalirana, kugawilana Kugawilana chikondi mosamanana eish Zomwe unalakwitsa ndi za make dzana Zomwe ndimalakwa umazipambana Kundiyimilila olo utangokhala Sindikuvala koma ase umandikhala Umandikhala nawe ndimakukhala Ineyo mpando wako ndipo umandikhala Mtima wanga kwa iweyo ndinamwaza Zoswelanaso mtima tinakanizana ndiye Ponda apo nane ndiponde apa Gwila apo nane ndikugwile apa Tivine stepe yokamanga wa muyaya Adziwe ndine wako iweso ndi wanga Tizikondana baby timakondana baby Iwe ndi wanga bae Ndiye undikonde konde konde Ndiye undikonde konde konde You are my favourite boy Kunamizana kunamizana Kumathawana kumbali tikufilana Kuzembelana mwa bodza ngati ana Kung'alula kuli kuwopa undikana koma Pano takula tasiya zachibwana Pano ndagula mphete kuti ukhale wanga Kulonjezana kulonjezana Pa makolo kuti sitizasiyana dziwa Zomwe unalakwitsa ndi za make dzana Iyi ikhale banja ndipo ukhale make wana Umandiyimilila olo utangokhala Zonse umakhumba nzakupatsa ine apa ndiye Ponda apo nane ndiponde apa Gwila apo nane ndikugwile apa Tivine stepe yokamanga wa muyaya Adziwe ndine wako iweso ndi wanga Tizikondana baby timakondana baby Iwe ndi wanga bae Ndiye undikonde konde konde Ndiye undikonde konde konde You are my favourite boy Give me loving on a daily Undikonde konde konde Nawe umandiyimilila ndikakhala pansi Umandichotsa ludzu ndikafuna madzi Ndiwe sindizasowa kanthu Ndiye ponda apa nane ndiponde apo Gwila apa nane ndikugwile apo Ponda apa nane ndiponde apo Gwila apa nane ndikugwile apo Tizikondana baby timakondana baby Iwe ndi wanga bae Ndiye undikonde konde konde Ndiye undikonde konde konde You are my favourite boy Give me loving on a daily Undikonde konde konde
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out