Lyrics

Ngati kumwambako kuli ma ukwati Mkayesetsa kukhala oyamba kukufusira Ukakhale mkazi wanga Mtima wako, maonekedwe Mayankhulidwe ngakhale poyenda Ndiwetu angel wangotsala mapiko hey Takula limodzi kuyambira umwana aha Tapanga chibwenzi moyo wathu onse aha Umkafuna banja Ine ndimkazemba aha Anzathu achangu angoti wanga buu wo-wo-woo Wamasuka mkazi uja Wakwatiwa bwezi langa Zikundiwawa kuti wandithawadi Moyo winawo mwinatu zidzayenda Wamasuka mkazi uja Wakwatiwa bwezi langa Zikundiwawa kuti wandithawadi Moyo winawo mwinatu zidzayenda Poti chitsime chimadziwika Kuti ndichakuya pomwe chawuma Mkazi wabwino umad'ziwa akapita Moyo winanwo ndidzayesetsa Kuchita zomwe utadzafune Poti panopa ndiwe mkazi wamwini (hey-hey-hey-hey) Takula limodzi kuyambira umwana aha Tapanga chibwenzi moyo wathu onse aha Umkafuna banja Ine ndimkazemba aha Anzathu achangu angoti wanga buu wo-wo-woo Wamasuka mkazi uja Wakwatiwa bwezi langa Zikundiwawa kuti wandithawadi Moyo winawo mwinatu zidzayenda (mwina, mwina, mwina, mwina) Wamasuka mkazi uja Wakwatiwa bwezi langa Zikundiwawa kuti wandithawadi Moyo winawo mwinatu zidzayenda Anyamata lero mukumaonjeza Kufuna banja koma kunjoya Mukamuvula mumamtaya ngazi sanza Iwe daughter wanga bwenzi lakolo Ngati akukonda adzadikilira Ndiwetu duwa lero mawa wafota oow Takula limodzi kuyambira umwana aha Tapanga chibwenzi moyo wathu onse aha Umkafuna banja Ine ndimkazemba aha Anzanga achangu angotipanga buu wo-wo-woo Wamasuka mkazi uja Wakwatiwa bwezi langa (bwenzi langa) Zikundiwawa kuti wandithawadi (zikundiwawa mama) Moyo winawo mwinatu zidzayenda (ngati uli ukwati mama) Wamasuka mkazi uja (ooh mkazi wanga) Wakwatiwa bwezi langa (ulendo) Zikundiwawa kuti wandithawadi (wapita) Moyo winawo mwinatu zidzayenda (oh iyo ma-ma-ma-ma)
Lyrics powered by www.musixmatch.com
Get up to 2 months free of Apple Music
instagramSharePathic_arrow_out