Lyrics

Kodi mesa munkatsutsa? Zoti ndi dolo Mutsutsa bwanji kwanzako inali true story? Kodi mesa munkatsutsa? Limakwana la fourty Osaphweketsa yanzako iliyose story Kodi mesa munkatsutsa? Zoti ndi dolo Mutsutsa bwanji kwanzako inali true story? Kodi mesa munkatsutsa? Limakwana la fourty Osaphweketsa yanzako iliyose story Ankandiseka nkavala zigamba Trouser lopanda lamba Nkhani zanga nkamakamba Ankaona lachokera banja langa Nkawawuza amasintha ndi masiku Chonde mundivele musawone msinkhu Koma ayi ankandiseka Ndipo ankati nzosatheka Koma Mulungu si nzako Program yake nde siyako Amadalitsa osasiyako Samapanga nawo zazisankho Kodi mesa munkatsutsa? Zoti ndi dolo Mutsutsa bwanji kwanzako inali true story? Kodi mesa munkatsutsa? Limakwana la fourty Osaphweketsa yanzako iliyose story Kodi mesa munkatsutsa? Zoti ndi dolo Mutsutsa bwanji kwanzako inali true story? Kodi mesa munkatsutsa? Limakwana la fourty Osaphweketsa yanzako iliyose story Munandisiya ndekha Pomwe ndinkakufunani osapezeka Maganizo, kupenga Mayesero ake nde sindinkavetsa Kugona ndi njala Kusowa kokhala Ku Kamba za nzeru ankayesa ndi misala Yah, yah, yah, yah, yah, yah Things change somehow Mulungu si munthu Sayiwala munthu Even when you're lonely Ndiyekha angakukonde Kodi mesa munkatsutsa? Zoti ndi dolo Mutsutsa bwanji kwanzako inali true story? Kodi mesa munkatsutsa? Limakwana la fourty Osaphweketsa yanzako iliyose story Kodi mesa munkatsutsa? Zoti ndi dolo Mutsutsa bwanji kwanzako inali true story? Kodi mesa munkatsutsa? Limakwana la fourty Osaphweketsa yanzako iliyose story (Loyal- Loyal Hustle; The Factory)
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out