Lyrics

Umangofuna tizicheza Paja umati ndimakuseketsa Tikamayenda kwa Milesa Anthu amangotisekelera Am I really in Love with You? Pena umangodipepelesa Am I really in Love with You? Pena umangodipepelesa Sindingakugawane ndi wina Kodi mawu aku lonjeza Nanga utaponda polakwika Ungadiuze ndisamale? Zomaswerana mtima Kundiuza ndiyiwale Ku lonjeza zosatheka mulibe mwako mu dikishonale Remember utagwada kuti ndidalire Unkati udzandikwatira kuti ndi dikirebe Are you really in Love with me? Olo Ukumangodipepelesa Are you really in Love with me? Olo nawe ukunditayitsa Are you really in Love with me? Olo ukumangodipepelesa Are you really in Love with me? Olo nthawi ukunditayitsa Chikondi chako Sindichiwona baby momwe uchikambira Chimandi talikira Ndipo mawu anga wako Amangosintha baby wakhumbira Ine nkhawi bii!!! Are you really in Love with me? Olo Ukumangodipepelesa Are you really in Love with me? Olo nawe ukunditayitsa Are you really in Love with me? Olo ukumangodipepelesa Are you really in Love with me? Olo nthawi ukunditayitsa (Umangodi umayi) (Umangondipepelesa) (Umangodi umayi) (Umangondipepelesa) are you really in love with me? Olo ukumangodipepelesa Are you really in love? Olo ukumangodipepelesa Are you really in Love?
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out