Featured In

Credits

COMPOSITION & LYRICS
Penjani Malata
Penjani Malata
Songwriter
Madalitso Kantema
Madalitso Kantema
Songwriter

Lyrics

Aseh Trappy! Fake friend Fake friend Fake friend Fake friend Oh no! Unkati uzandigwila nkono Uzandithandiza nzikhomo ey Pano wandisiya choncho ndiwe fake friend Fake friend ey fake friend ey Fake fake friend ey fake friend ey Chariz! Fake Unanditsika kundituluka Unaiphula unatukuka Kundiiwala osandikumbuka Kusiya halla mutatola thumba Ah I thought you my dawg I thought you my friend Unkapangilanji pretend Ankakudziwa padeni, unkagwilizanaso ndi masten Komwe tachoka tachokako ndikutali Tokha tokha kumaikana carnal mind Oh no! Unkati uzandigwila nkono Uzandithandiza nzikhomo ey Pano wandisiya choncho ndiwe fake friend Fake friend ey fake friend ey Fake fake friend ey fake friend Fake Mesa unali nzanga wa ponda apa mpondepo Koma wandisewela ngati chiukepo Tinkakondana ngati fulemu ndi chitseko Koma pano wasitha nyengo ndiwe mphepo Unali wabodza (umanama) Kumapeka nkhani kumandinamiza Ndiwe ride or die Utasunga ka mpeni Ku phasa kumati ine ndi khale Why were you lying? Sunandipatseko olo ma sign Kupita Kumbali kumakakambako za ine Kuwauza adani zofooka za ine Oh no! Unkati uzandigwila nkono Uzandithandiza nzikhomo ey Pano wandisiya choncho ndiwe fake friend Fake friend ey fake friend ey Fake fake friend ey fake friend ey Fake Fake friend Fake friend Fake friend Fake
Lyrics powered by www.musixmatch.com
instagramSharePathic_arrow_out